Ndife Mzika Zakwa Chinsapo

Ndife Mzika Zakwa Chinsapo Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Ndife Mzika Zakwa Chinsapo, Social Media Agency, Lilongwe.

Monga mzika zakwachinsapo iyiyi yabaya 😭
07/12/2024

Monga mzika zakwachinsapo iyiyi yabaya 😭

Tatiyeni tikhale anthu ozindikira komanso ophunzitsika, zachitikazi taonetsa umbuli kwambiri komanso ndizomvetsa chisoni...
09/09/2024

Tatiyeni tikhale anthu ozindikira komanso ophunzitsika, zachitikazi taonetsa umbuli kwambiri komanso ndizomvetsa chisoni..

Monga chinsapo tiyeni tidzitolele mmachitidwe athu a zinthu

Rip nchimwene

22/08/2024

Chinsapo chafumbi 😂😂🙌 kwathu nkonkuno

Mukadzaona aka mudzakhote, nudzayambira kupeza four ways pamajiga... Kenako azayende bwanji? Pelekani map ena
06/03/2024

Mukadzaona aka mudzakhote, nudzayambira kupeza four ways pamajiga... Kenako azayende bwanji? Pelekani map ena

03/03/2024

Momujatu muchinsapo

Nayenso Jones Khombe watenga yake kufuna kuinyadira kuti iwowo ndi Mzika Zakwa chinsapo
18/02/2024

Nayenso Jones Khombe watenga yake kufuna kuinyadira kuti iwowo ndi Mzika Zakwa chinsapo

Mzika ya kwachinsapo Ku town
18/02/2024

Mzika ya kwachinsapo Ku town

Naye oimba uyu Chiksy pozindikira kuti naye ndi MZIKA wapeza yake yoti azivala akamapita Ku show ...0884644526 kuti mupe...
12/02/2024

Naye oimba uyu Chiksy pozindikira kuti naye ndi MZIKA wapeza yake yoti azivala akamapita Ku show ...

0884644526 kuti mupeze yanu

12/02/2024

Monga Mzika zakwachinsapo, inuo mukagula T shirt yi ifeo ndalama zakezi cholinga chake ndichothandiza anthu omwe akuvutika muchinsapomu...

Ndife Mzika.... Anthutu akutchena kunjaku ......
10/02/2024

Ndife Mzika.... Anthutu akutchena kunjaku ......

Akabanza athu mumatiimirira ..Wawa👋 pa rank yapamanda apo.. tchulani rank yanjinga yomwe munayandikana nayo
08/02/2024

Akabanza athu mumatiimirira ..Wawa👋 pa rank yapamanda apo.. tchulani rank yanjinga yomwe munayandikana nayo

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ndife Mzika Zakwa Chinsapo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share