31/10/2025
Immediate Hiring 📢📢
Muli ndi experience yotsuka ma galimoto kugwirisa ntchito machine? Mumatha ku phika ma hotdogs 🌭 Shawarma? Mwayi wanu uwu!!! Gama Express Carwash akufuna anthu awili ku shop yawo yaku Lilongwe. Awuzeni anzanu alembele ngati alindi zofunikazi. For more information Call 0899 99 62 00 mawa kuyamba ntchito
Benefits: Free Lunch, Uniform & Day off