Ice beats studios

Ice beats studios A Home of Quality Music

05/09/2025

ZILI PATI

03/09/2025

Kukubwera chinyimbo china choopsa guys, ZILI PATI.

Ice beats studio

Mwayenera Yesu by Chikonzero Mwansambo still being downloaded. Anthu akuifila. Lets show love. Lets reach 1k downloads f...
29/08/2025

Mwayenera Yesu by Chikonzero Mwansambo still being downloaded. Anthu akuifila. Lets show love. Lets reach 1k downloads for him to win 5pin. We are at 123 downloads. We are closing this chance tomorrow 23:59. Link in the comments.

ICE BEATS

29/08/2025

Kodi zomwe munatilonjeza zija zili pati? Anthu andale amwene, aaa.

Rico Dee ft Ice cool

Adah awa amatha kuimba aise ee. Ulemu wako Rico Dee kapena kuti Achina4cs
28/08/2025

Adah awa amatha kuimba aise ee. Ulemu wako Rico Dee kapena kuti Achina4cs

28/08/2025

Successful projects so far

Ubwerere - Chegoh ft Ice cool (Ice beats studio)
Akubwera Yesu - Chikonzero Mwansambo (Ice beats studio)
Mwayenera Yesu - Chikonzero Mwansambo (Ice beats studio)

Links in comments

25/08/2025

Ife tikumvera Mwayenera Yesu
Beat by Ice beats studio
Audio by Ice beats studio

Ice beats studio more firee 🔥💥🎶😎

Sunday lafika lokha. Tadza nacho chinyimbo chatsopano choimbidwa ndi Chikonzero Mwansambo chomwe akuti Mwayenera Yesu. T...
24/08/2025

Sunday lafika lokha. Tadza nacho chinyimbo chatsopano choimbidwa ndi Chikonzero Mwansambo chomwe akuti Mwayenera Yesu. Tachimvereni, mumenye like komanso comment. Link ili mu comment section. Osaiwala kuti ma downloads akakwana 1k pomafika next Sunday, nyimboyi ilandira k5000 award.💥💥

ICE BEATS STUDIO

Hello peoplePakatipa panali zochedwetsa zingapo kuti nyimbo zizituluka. Kwakukulu, timapanga zoti programu ija ya Award-...
20/08/2025

Hello people

Pakatipa panali zochedwetsa zingapo kuti nyimbo zizituluka. Kwakukulu, timapanga zoti programu ija ya Award-for-1k Downloads ikhazikike, ndye zatheka. Chomwe chizichitika nchoti tizikufilitsani nyimbo zojambulidwa ku Ice Beats Studio Sunday iliyonse. Nyimboyo tiziiponya pa website (pakali pano tikuponya pa NyasaBeats.com). Ikamafika Sunday inayo,12 am, eni nyimbo ija aziyenera kulandira award ya Mk5000 ngati nyimbo yawo yafika 1k downloads.

Tiyeni tikonzeke kumvera nyimbo ya Mwayenera Yesu Sunday likubwerali.

ICE BEATS STUDIO🔥

Mu nyengo ya ndale ngati ino, dziko lonse ladalira inu mbuye. Mwayenera Yesu🔥
20/08/2025

Mu nyengo ya ndale ngati ino, dziko lonse ladalira inu mbuye. Mwayenera Yesu🔥

Pakutsalabe zinthu zingapo zoti zichitike kuti tifile nyimbo yatsopano ya Chikonzero Mwansambo yomwe mutu wake ndi Mwaye...
13/08/2025

Pakutsalabe zinthu zingapo zoti zichitike kuti tifile nyimbo yatsopano ya Chikonzero Mwansambo yomwe mutu wake ndi Mwayenera Yesu. Tikufuna mukaimvera, muzimuke nayo nyimbo ya gospel yokomayi.
Ulemu wawo Achiu Visuals potikungira artwork yokongola ya nyimboyi🔥

Yesu akuyeneradi ulemu wonse. Sunday likubwerali. Zaambuye izi🔥
06/08/2025

Yesu akuyeneradi ulemu wonse. Sunday likubwerali. Zaambuye izi🔥

Address

Mitundu
Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Ice beats studios posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share