Love Novels Malawi

Love Novels Malawi Welengani nkhani zoiwalitsa mavuto koma osaiwala kupanga like page-yi.

Sindingakwanitse ndekha kukolopa nyanja tabwelan fast fast
30/10/2025

Sindingakwanitse ndekha kukolopa nyanja tabwelan fast fast

27/10/2025

Kod mwanva? Bungwe la NASA lomwe limaona za mlengalenga mpaka lero silidatulutsebe zinthuz za mwala omwe ukuyenda mlengalenga (astroid) omwe ena ak*t nd chombo cha ma Alien zomwe robot wawo waku mars adajambula pano zkunveka k*t chombocho mayendedwe ake ndiokakitsa pamene bungwe la NASA silik*tulutsa zithuz ikamadzafik december chikhala chikudzadutsana nd dziko lapansi kod mukuganiza zomwe ena akuganiza?
Page ino simakhulupilira zot kuli ma Alien ndpo smakhulupilira k*t kuli space komaso simakhulupilira zot dziko ndlozongulira

Ry this pezan google gemin appIkan pungan upload nkhope yanu ndkulemba A funny and awkward moment inside an elevator — o...
27/10/2025

Ry this pezan google gemin app
Ikan pungan upload nkhope yanu ndkulemba A funny and awkward moment inside an elevator — one man standing confidently in the center wearing a gray t-shirt and cap labeled “Jackie,” while everyone around him covers their noses and mouths, laughing and reacting to a bad smell. The setting is a modern elevator with metallic walls, warm lighting, and a gold-framed mirror behind them. The mood is humorous and candid. Zioneka chonchi pali nkhope yanu..... Kwa amene mukukaikila onani original picture

Mwaona? Mukumafunsa ku inbox mmalo mot ena aphunzile nawo p***a tiyen tipange comment komaso follow Love Novels Malawi M...
23/10/2025

Mwaona? Mukumafunsa ku inbox mmalo mot ena aphunzile nawo p***a tiyen tipange comment komaso follow Love Novels Malawi Mmene mungapangire chithunzi chanu k*t chioneke chonch ku inbox kudzitchenetsa.... Kudziyika kumalo kot sudapiteko

Inu zovaya photoshoot pano zidachepa nkhope yanu yokhayo AI kuipanga zinthu kupezeka komwe inuyo mungafune pangan follow...
23/10/2025

Inu zovaya photoshoot pano zidachepa nkhope yanu yokhayo AI kuipanga zinthu kupezeka komwe inuyo mungafune pangan follow k*t mudyele kugwilitsa ntchito Nano Banana AI

Prompt 👇
16K ultra-realistic cinematic 9:16 — luxury European hotel lobby.
Subject: same man, 5'3", sitting on sofa, legs crossed, relaxed mood.
Outfit: brown drop-shoulder T-shirt, olive shorts, colorful Adidas sneakers.
Lighting: golden warm tone, cinematic background depth.
Face and hair styles exactly uploaded photo.

Trending Photo Editing Tutorial with Gemini | Free AI Photo Editing

Ngat mukufuna kuphunzila kupanga edit zithunzi zanu nd Google gemin pangan follow komaso comment, yesan aka k*t pakhale ...
22/10/2025

Ngat mukufuna kuphunzila kupanga edit zithunzi zanu nd Google gemin pangan follow komaso comment, yesan aka k*t pakhale nkhope yanu koma mupezeke muli kwina pangan download google germin ikan pic ndpo lemban izi

By using the exat face uploaded
Cinematic 3:4 shot of me standing still on a rainy city sidewalk. I'm wearing an oversized black T-shirt, baggy pants, and sneakers. Holding an umbrella with one hand while rain pours heavily around me. Moody lighting, shallow depth of field, reflections on wet pavement, soft backlight halo. Film still look, slightly desaturated colors. Focus on emotion, solitude in the storm.













27/08/2025

Ana a 2 sauzande Ak*t kupanga timagulu tofuna kumutuluka driemo 🤣🤣🤣🤣inu driemo anakamba chilungamo mwachidule anabisa nanga akadanena k*t rash anajambula p**n ndkuiyoka online ndcholinga chot apange promo nyimbo a rash akadalira motan? Onse nd abho komano arashly vuto amanveka mofanana nthaw zonse ali nd voice yabho komano a zisintha ko mawu

Address

Lilongwe

Telephone

+265885381781

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Love Novels Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category