
07/06/2025
Let's answer these questions aswel!π
This is a right question
Our industry is not bringing promoting many young artists because ma big artists akumachulutsa kunamiza anawa as a results sakupita patsogolo.....
2024 kunatuluka ma artist abho abho komanso mafana chifukwa kunsana kwao kuli anthu akulu akulu.
Chinanso Malawi imatulutsa 0.01% Yama artists a new Chaka chilichonse chifukwa aakuluwo alibe kamtima kokweza ma percentage ama upcoming artists.
We need to do something!
:- written by A Pre.