Malawi Urban Trends

Malawi Urban Trends Creative vision

25/07/2025

Shaaaaa🤔
゚viralシfypシ゚

25/07/2025

Jolasto

25/07/2025

Don't promise what you can't give.....
゚viralシfypシ゚ ゚viralシ

21/07/2025

Chinyimbo iweeeee.
゚viralシfypシ゚ ゚viralシ

Jetu....
30/06/2025

Jetu....

The is all about praising your partner for things they're doing for you

 Mkulu wa gulu la nkhondo mdziko lino la MDF, General Dr. Paul Valentino Phiri wati nthambi ya chitetezoyi ndi yodzipere...
28/06/2025


Mkulu wa gulu la nkhondo mdziko lino la MDF, General Dr. Paul Valentino Phiri wati nthambi ya chitetezoyi ndi yodzipereka kuteteza anthu mosakondera monga mwa malamulo ndipo ikuwunika momwe asilikali anagwilira ntchito pa zionetsero zomwe zinachitika ku Lilongwe Lachinayi.

General Valentino Phiri wati MDF ikudziwa udindo wake ndipo pali zambiri zofunika kuti iwunikire bwino zimene zinachitikazo.

Magulu ena akudzudzula MDF ati chifukwa asilikali ake amangowonelera zigawenga zimene zinali ndi zida monga zikwanje zidasokoneza zionetserozo komanso kumenya omwe amatsogolera a Sylvester Namiwa.

(by Sam Banda-Lilongwe:06/28/25)

President Dr Dalitso Kabambe anapita kukazonda Mr Silvester Namiwa madzulo ano. Thank You Dr Dalitso Kabambe your a very...
28/06/2025

President Dr Dalitso Kabambe anapita kukazonda Mr Silvester Namiwa madzulo ano. Thank You Dr Dalitso Kabambe your a very active leader, the Man Malawians want now.

This is bad.....
26/06/2025

This is bad.....

26/06/2025

These people are not serious mpaka police kumathawa?? Com on Malawi.....

26/06/2025

Izizi nzachibwana Malawi police aaaaah.......

phyzix new hit...
26/06/2025

phyzix new hit...

Phyzix, It's Only Entertainment (IOE) Artist/CEO delivers his brand-new music video for his 2025 song, 'SAUCE' ft. Classick & Quest. ...

Address

Lilongwe

Telephone

+265883637372

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Urban Trends posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi Urban Trends:

Share