Channel for All Nations Media

Channel for All Nations Media Official page for Channel for All Nations Media. The aim of this page is to promote the vision and m

08/10/2025

RED CARD

08/10/2025

THUMBA LA M'BUSA

05/10/2025

ICA SUNDAY SERVICE | 5TH OCTOBER 2025

 Mbali inayi kampani ya phone za m'manja ya TNM yawuza ma kasitomala ake kuti akoze bwinobwino, chifukwa kampaniyi ikwez...
03/10/2025


Mbali inayi kampani ya phone za m'manja ya TNM yawuza ma kasitomala ake kuti akoze bwinobwino, chifukwa kampaniyi ikweza mitengo ya ntchito zake.

Kampaniyi yati ichita izi pofuna kuti ikhalitse ikutumikira nzika za dziko lino komaso kuti izipereka ma service apamwamba ka ma kasitomala ake.

Iyo yati yafika pa ganizoli itatutumuka ndi kukwera kwa zinthu pa nsika maka zipangizo zomwe imagwiritsa ntchito popereka ntchito zake kwa ma kasitomala.

 PANSIKA PAKHWITHIMA ZEDI.Nayo kampani yopanga sugar m'dziko muno ija ya Illovo, yawona kuti isadeweze pochita zinthu, n...
03/10/2025


PANSIKA PAKHWITHIMA ZEDI.

Nayo kampani yopanga sugar m'dziko muno ija ya Illovo, yawona kuti isadeweze pochita zinthu, ndipo pomwe kumada tsiku lalero pa 3 October 2025, sugar wa kampaniyi wakwera mtengo.

Kampaniyi yalengeza izi kudzera pa kalata yomwe, ndipo iyo yati yachita izi polingalira momwe pansika palili maka kumbali yamalonda.

Zateremu zika ziyamba kugula pakete ya sugar yolemela kilogram imodzi pa mtengo wa K3,700.

Pa 1 October bungwe la Malawi Energy Regulatory Authority MERA lidakwezaso mtengo wa mafuta agalimoto pazifukwa ngati zomwezi.

03/10/2025


The women's manifesto movement has regarded the September 16 Parliamentary elections as a success, stating that the election reflected their desire to empower more women in key decision-making positions in government.

In an interview with Channel for All Nations, Lingalileni Mihowa from the women's manifesto movement stated that the movement notes the increase in women securing Parliamentary seats, a move she regarded as a milestone towards women empowerment.

Despite encountering several setbacks along the way during the campaign, such as funding constraints, Mihowa praised citizens for their unwavering support lent through resources, emotional boosts, as well as voting for them on the ballot.

Meanwhile, Mihowa has appealed for continued collaboration among stakeholders in promoting women's rights and empowerment to achieve common goals.

In the immediate parliamentary elections, about 48 women have been voted in as members of parliament to serve citizens in their constituencies in the next 5 years.

 Wapampando wa gulu lomwe lakoza phwando la nyimbo zotsitsimutsa miyoyo lomwe  akulitcha kuti Summer Gospel concert,  Za...
03/10/2025


Wapampando wa gulu lomwe lakoza phwando la nyimbo zotsitsimutsa miyoyo lomwe akulitcha kuti Summer Gospel concert, Zachariah Jazman, watsindika kuti tsopano anthu okonda nyimbo zauzimu azikondwa chakam'chaka ndi mapwando akuluakulu a nyimbo zawuzimu ngati muja achitira wena oyimba nyimbo zachitayiko pang'ono, mochemerera zachibwana.

Malingana ndi Jazman tsopano iwo agalamuka kuti azichititsa mapwando otere koma yaphindu mu uzimu, ndipo iwo achita izi koyamba m'dziko muno mu mzinda wa Lilongwe.

Magulu oyimba ngati mayi aja a Takulandirani kuno ku Masintha chitsitsimutso choir, Milefa sisters, Magie Mangani , Apostle Norman Phiri , Joseph Zalinga ndi ena omwe atsekulire izi chaka chino pa 9 November pano.

Momkelamkela kuphweketsa ndi kutendera bwino phwandoli, makosanawa lero achita m'gwirizano ndi kampani ija ya Kwenda.Co, pofuna kuti anthu athe kupeza ma tikiti odzalowera ku phwandoli mophweka zedi.

Phwando la mayimbidweli lidzachitika pa 9 November 2025 ku Sheafer ICA Marquee mu mzinda wa Lilongwe.

Wolemba: Obed Samison.

03/10/2025

THUMBA LA'BUSA 2025

Address

Corner Of Paul Kagame Road And The M1
Lilongwe
1220

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 08:00 - 17:00
Sunday 08:00 - 17:00

Telephone

+265999600142

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Channel for All Nations Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Channel for All Nations Media:

Share