06/07/2023
After kuonera game ya Flames yomwe Alick Lungu wakhala man of the match basitu kuyamba kusinza pa mpando pompo... mkati mosinza muja kuyamba kulota Dreimo atamenya collabo ndi Jah Prayser waku Zimbabweyu.. Koma nyimbo inavuta iyo... sindimalota zabodza ine.. chinachake chichitika...