04/12/2025
Zikuchitikira mu Lilongwe ndi Quick Mai Delivery kungowaimbira phone ndikunena Zinthu zomwe mukufuna kuti akugulireni kuma sitolo osiyana-siyana, akumagula zinthuzo ndikukubweretserani.
Mukhoza kuwaimbira phone pa nambala iyi.
0983 02 09 11
Musavutike ndikuyenda kukagula pizza, ayimbireni phone ndipo akuthandizani.
Quick Mai Delivery, ali pano kukutumikirani.