VOY Television

VOY Television Empowering Young Minds, Amplifying Their Voices

Kodi ndinu Oyimba kapena wa luso lililonse?Tipezeni ife a VOY Television kuti tichitepo gawo lathu potukula luso lanu 🔥M...
24/09/2026

Kodi ndinu Oyimba kapena wa luso lililonse?

Tipezeni ife a VOY Television kuti tichitepo gawo lathu potukula luso lanu 🔥

Musanyalanyaze tiyimbileni pa 0982010806
Luso ndi Golide!

"AMPLIFYING VOICES OF YOUNG PEOPLE"

In the pictures: Spin lou TE and chapo 6ix
Musicians.

Kodi mukufuna ma service apamwamba pa project yanu?Yankho lanu ndi Akatswiri a Royal Shield General Service Iwowa akupez...
24/09/2026

Kodi mukufuna ma service apamwamba pa project yanu?
Yankho lanu ndi Akatswiri a Royal Shield General Service
Iwowa akupezeka mu mzinda wa Lilongwe kwa Chinsapo ndipo ali ndi kuthekera kofikira boma lililonse muno M'malawi 🇲🇼
Musachedwe lumikizanani nawo pa 0997719588/0880455496
'SHIELDING WHAT MATTERS, SERVICING WHAT YOU NEED"

Kwabwera chi Mwayi chofuna kutukula luso la wachinyamata ndi ukadaulo wapamwamba pa Utolankhani 🇲🇼🔥Dzipezeleni malo ku M...
18/09/2026

Kwabwera chi Mwayi chofuna kutukula luso la wachinyamata ndi ukadaulo wapamwamba pa Utolankhani 🇲🇼🔥
Dzipezeleni malo ku Malawi Institute of Journalism - MEDIA Training kuti January 2027 Intake ikuikeni Ntika🤙

Applicants can use the link below 👇 https://forms.gle/RY9NXg6kPH4qxWZf9

Tamva kuti Achinyamata ena mumapsepsa kuwelenga Newspaper akuti nkumati zachigogo  Komano mukuchedwa kobasi 😎Auzeni anth...
17/09/2026

Tamva kuti Achinyamata ena mumapsepsa kuwelenga Newspaper akuti nkumati zachigogo Komano mukuchedwa kobasi 😎
Auzeni anthuwa Director Favour Kapindula 🤣🤣

Lero kwaphulika chi Umboni 🤔Inu maganizo anu ndiotani?
15/09/2026

Lero kwaphulika chi Umboni 🤔
Inu maganizo anu ndiotani?

09/09/2026

Manthu wa ma Television!
🇲🇼🔥

Happy birthday Honorable Kendall Kamwendo.
02/09/2026

Happy birthday Honorable Kendall Kamwendo.

CHAMPIONS 🔥
30/08/2026

CHAMPIONS 🔥

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when VOY Television posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category