Nkhani Izitha

Nkhani Izitha Entertainment

Religion was brought to Afrika as Second slave trade.Bible lonse kapolo lemekeza mbuye wako.Kapolo= Afrikan Black manMbu...
17/05/2026

Religion was brought to Afrika as Second slave trade.

Bible lonse kapolo lemekeza mbuye wako.
Kapolo= Afrikan Black man
Mbuye wako=White people

That's why you see a lot of churches but few hospitals poor schools poor roads

that's why you see alot of vaccines and a lot of deaths
simungapange sense.

You know why?

because you're in the system.

You have been manipulated

That's why you go and Vote every 5 years but zero development
Vuto after Vuto. They're not in control. Alipo amene anapanga control dzikoli

With all these churches simene tikuvutikira simene anthu akudwalira simene anthu akufera what are you doing in the church?

Kusala kudya basi?

kugula Malo kumanga ma tchalitchi basi?

Mangani zipatala mangani ma sukulu mangani polisi limbikitsanani ulimi yambani ulimi wa serious muthana ndi njala osati kukwera phiri.

For how long?

15/05/2026

Despite the wrong doings Dr Lazarus Chakwera and his party did to Malawians

they do not deserve that kind of treatment.

Koma being the country where people celebrate someone's fate people are busy clapping hands.

Chifukwa anthu ake ambiri mitu yawo ndiyouma Samatha kuzindikira chabwino ndichoipa akusekelera zopusazi.

Dziko loika ndale patsogolo Malo mwa chitukuko palipose padaola.

Mwawasiya osawaitana ku celebration ya first president chifukwa chiyani?

Sadakakamire akulorani mumalize zanuzo iwowo pamapeto pakepo apite akaone Manda Pali vuto?

Magayez a DPP tikamati boma sitimayendetsa ndi mkwiyo timanena izi.

Infact Kamuzu was first president of the nation not party

mukuganiza bwanji?

Kuuma Mutu kotani?

15/05/2026

Zimene apanga apolisi zija ndikuuma mutu

mwawaletsa kupanga nao msonkhano avomera
apanga wawo mukuwatchingaso?

02/05/2026

Jomo ananyanya kupopedwa 😀😂😂
Inu kumaona zinazi 😜😜😜

How do you feel?😳😳
01/05/2026

How do you feel?😳😳

27/04/2026

Sponsor wake wa Mtima tu😂😂😂😂

20/04/2026

Incase you missed it from Alexious kamangila

20/04/2026

Barber man uja amasewera ma business ake ndima biggie omwewa nkona akumuikira kumbuyo

Ifewo tikhale ansanje

20/04/2026

Black Market MK22 000 🤣😂

Proven leadership

20/04/2026

mafuta mwakweza koma bwezi akupezeka 😂😂😂😂

Kufinyidwa olo achina Kachamba akusowa zonena

Address

Lilongwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Nkhani Izitha posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category