LUANAR FM

LUANAR FM The Voice that Matters - Live on 99.6/99.8 MHz
Your station for agriculture, development, education, innovation & entertainment.

Bungwe la Federation for Disability Organizations in Malawi (FEDOMA) laphunzitsa achinyamata aulumali momwe angapangire ...
27/09/2026

Bungwe la Federation for Disability Organizations in Malawi (FEDOMA) laphunzitsa achinyamata aulumali momwe angapangire ma bizinesi azaulimi ndicholinga choti athe kudziimira paokha komanso kuthandiza pa chitukuko cha zaulimi ku madela awo.

Poyankhula atatha maphunzilowa, mmodzi mwa akuluakulu ku FEDOMA a Ganizani Gabriel anati achinyamata aulumali sakuyenera kudziyan’ganira pansi poti nawonso ali ndi gawo loti achite potukula madera awo kudzera mu ulimi kapena bizinesi.

Achinyamata 14 ndiwo afikiridwa ndi maphunzirowa omwe anali a masiku atatu ndipo anachitikira ku Mitundu m’boma la Lilongwe.

Maphunzirowa anakonzedwa pansi pa polojekiti yomwe ikufuna kutukula achinyamata aulumali powapatsa luso losiyanasiyana ndipo ikulandira thandizo kuchokera ku Youth Entrepreneurship for Future Food of Agriculture (YEFA) kudzera ku Alliance for Green Resolution in Africa (AGRA).

Wolemba: Kenneth Luciano

24/09/2026

To all the reggae lovers!
Join Isaac tomorrow on the Friday Reggae Jam session from 4pm to 5pm as he will bring you some good reggae music to take you into the weekend.
99.6Mhz The Voice that Matters

Hello! Mwaliyamba bwanji tsiku lanu lero lachiwiri pa 15 September? Tiyeni tikumane ndi Taim Jimmy mu program ya Malonje...
15/09/2026

Hello! Mwaliyamba bwanji tsiku lanu lero lachiwiri pa 15 September? Tiyeni tikumane ndi Taim Jimmy mu program ya Malonje 9 koloko ino pa FM. Pelekani Malonje pa wailesi poyimba phone kapena kutumiza uthenga wa m'manja pa 0980 440 556 kapena 0890 891 940.
Bwerani tiyipatse moto.
FM Moto kuti Buuuuuu!!!!

GOOD VIBES FOR YOUR MORNING!There’s nothing like starting the day with great music, positive energy and the right compan...
10/09/2026

GOOD VIBES FOR YOUR MORNING!

There’s nothing like starting the day with great music, positive energy and the right company on the airwaves.

Sylvia is bringing the good vibes this morning on LUANAR FM, keeping you entertained, connected and ready to take on the day.

Tune in on 99.6 & 99.8 MHz
Good music. Good energy. Good morning.

LUANAR FM — The Voice That Matters.

EKHAYA FC PART WAYS WITH HEAD COACH CHATAMAEkhaya FC have parted ways with First Team Head Coach Enos Chatama with immed...
08/09/2026

EKHAYA FC PART WAYS WITH HEAD COACH CHATAMA

Ekhaya FC have parted ways with First Team Head Coach Enos Chatama with immediate effect.

The club says the decision follows a review by its leadership and is in the best interest of the team and its objectives for the season and beyond.

The club leadership has thanked Chatama for his contribution during his time at the club, having guided Ekhaya to a top-eight finish in his first season and winning the Airtel Top 8 trophy.

Meanwhile, Fundi Akidu will take charge as interim coach, assisted by Moses Chavula, as the club begins the process of finding a new head coach.

By Isaac Songola

HAPPY NEW MONTH!Welcome to September with LUANAR FM!A new month means new beginnings, fresh energy and more reasons to s...
01/09/2026

HAPPY NEW MONTH!

Welcome to September with LUANAR FM!

A new month means new beginnings, fresh energy and more reasons to stay tuned to the station that keeps you connected.

Stay tuned. Stay informed. Stay entertained.

LUANAR FM — The Voice That Matters.

MALAWI SEEKS STRONGER LINKAGES BETWEEN SOCIAL PROTECTION AND AGRICULTUREMalawi is seeking stronger linkages between soci...
01/09/2026

MALAWI SEEKS STRONGER LINKAGES BETWEEN SOCIAL PROTECTION AND AGRICULTURE

Malawi is seeking stronger linkages between social protection and agriculture to improve support for vulnerable communities and livelihoods.

As part of this effort, LUANAR, through its Centre for Continuing Education and Professional Development (CCEPD), in partnership with the Government of Malawi and the United Nations Global Accelerator Joint Programme, is conducting a five-day Training of Trainers for social protection and agriculture personnel from nine districts in the Southern Region.

The training, which started on Monday in Blantyre, is piloting a new LUANAR short course designed to equip practitioners with skills to better integrate social protection programmes with agricultural interventions.

The training will also be rolled out in other regions in the coming weeks.

By Isaac Songola

COWBOYS RIDE INTO HISTORY! 🤠🏆Ekhaya FC have done the unthinkable!The Airtel Top 8 debutants have stunned the football fr...
30/08/2026

COWBOYS RIDE INTO HISTORY! 🤠🏆

Ekhaya FC have done the unthinkable!

The Airtel Top 8 debutants have stunned the football fraternity, beating Mighty Wanderers 2–1 in the final at Bingu National Stadium to lift the trophy in their first-ever appearance in the competition.

And what a journey it has been for the Cowboys.

They came into the tournament knowing they would have to face giants — and they did exactly that. First, they knocked out Nyasa Big Bullets. Then came Blue Eagles. And in the final, they finished the job against Mighty Wanderers.

Three giants. Three statements. One trophy.

Ekhaya only earned their place in the Top 8 after an impressive debut season in Malawi's top-flight league, finishing among the country's best eight teams.

Now, just one season after arriving in the elite league, the Cowboys have gone all the way.

First appearance. First final. First trophy.

Ekhaya FC have arrived — and they have arrived in style.

By Isaac Songola

Nduna ya za ulimi olemekezeka a RosaMbilizi ayamikira sukulu ya ukachenjede ya LUANAR pobwera ndi njira za ulimi za mako...
27/08/2026

Nduna ya za ulimi olemekezeka a Rosa
Mbilizi ayamikira sukulu ya ukachenjede ya LUANAR pobwera ndi njira za ulimi za makono komanso zosavuta kugwiritsa ntchito.

Ndunayi yanena izi pa mwambo wotsegulira
chionetsero cha zaulimi cha chaka chino ku Trade Fair mu mzinda wa Blantyre.

A Mbilizi adati sukulu za ukachenjede ndi zofunikira kwambiri popititsa patsogolo ntchito za ulimi m'dziko muno, ndipo adayamikira sukulu ya LUANAR pochilimika pa nkhani za kafukufuku yemwe akubweretsa njira zamakono komanso zosavuta kugwiritsa ntchito.

Mwa zina, sukulu ya LUANAR ikuwonetsa feteleza, mankhwala otetezera mbeu komanso njira zoyezera matenda ku ng’ombe za mkaka zomwe zili zotsika mtengo komanso zosavuta kupeza kwa alimi.

Chionetserochi, chomwe chayamba pa 27 August, chidzatha loweruka, pa 29 August, 2026.

Wolemba: Isaac Songola

Mfumu yaikulu Chadza yochokera m'boma la Lilongwe yalimbikitsa anthu am'dera lake kuti achilimike pa nkhani ya ulimi kut...
26/08/2026

Mfumu yaikulu Chadza yochokera m'boma la Lilongwe yalimbikitsa anthu am'dera lake kuti achilimike pa nkhani ya ulimi kuti apitilire kukhala achitsazo pa nkhani ya zaulimi .

Izi zayankhulidwa lachiwiri pa mwambo opereka chikho cha za ulimi ( Agriculture Trophy) omwe unakozedwa ndi a T/A Chadza komaso mafumu ozungulira m'dera lawo.

"Mfumu singalamulire anthu amene ali ndi njala, choncho anthu am'dera lino mukuyenera kulimbikira ulimi komaso mukhale m'magulu kuti muzigula mbewu mosavuta."

Pamwambowu alimi amene achita bwino alandira mphotho zosiyanasiyana monga njinga yakapalasa, wilibala , matumba a Fertilizer ndizina zambiri.

Ndalama zokwana 4.3 million kwacha ndizomwe zagwira ntchito pokonza mwambuwu.

Olemba: Milcah Chimoyo Jabes
# LUANAR FM

Address

219
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when LUANAR FM posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category