23/07/2026
Anthu amalakhula ndipo alakhura koma sizingasithe chilichonse chifukwa zagwa zagwa basi..
Koma tafotokozani kodi mphazi linali size chani..?
Nde phazi ena akutinso mfuti iwe mwini uwafotokozela motani anthu alitchelu kufuna kumva zambiri enanso akufuna ataona chifukwa akungomva