Dalitso kachambo

Dalitso kachambo Success come to those who may wait
And chance never come alone we creat😉

Happy follow-versary to my awesome followers. Thanks for all of your support! Owen Bornfece
04/09/2025

Happy follow-versary to my awesome followers. Thanks for all of your support! Owen Bornfece

Save!!!!
27/08/2025

Save!!!!

17/01/2025



Ambali ya boma alephera kubweretsa mboni pa mlandu omwe gavanala wa DPP mchigawo cha kuvuma yemwenso ndi phungu wa nyumba ya malamulo kudera la pakati pa boma la Machinga a Daud Chikwanje akuyankha.

Izi zachititsa kuti oweruza milandu a Maxwell Boaz aimitse mlanduwu kufikira pa 11 mwezi wa mawa.

Mwa zina a Boaz achotsanso chilango cha belo chomwe a Chikwanje adapatsidwa kuti adzikaonekera ku bwalo la milandu lachisanu lirilonse ndipo mmalo mwake a Chikwanje sadziyenderaso beloyi.

Koma poonekera ku bwaloli a Chikwanje aukana mlandu oyankhula mawu omwe ali ndi kuthekera kodzetsa chisokonezo omwe akuzengedwa.

A Chikwanje adamangidwa mwezi wa September kutsatira kanema wina yemwe anaonetsa iwo akuyankhula pa msonkhano wina m'boma la Machinga.

Wolemba Blessings Tambala.

12/01/2025

Incase you missed this Arthur Peter MutharikaDemocratic Progressive Party - DPP PRESSHon. Alfred Gangata - DPP Vice President CentreDPP-DEMOCRATIC PROGRESSIVE PARTYHon Kamlepo Kalua

12/01/2025
12/01/2025

His Royal Majesty Ngwenyama Inkosi Ya Makhosi Gomani VHis Royal Majesty Inkosi ya Makhosi M'mbelwa VDemocratic Progressive Party - DPPArthur Peter Mutharika

12/01/2025

🔥🔥🔥🔥akumuopa munthuyiDPP PRESS

Address

Mtagaluka Soweto
Mangochi

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Dalitso kachambo posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share