H pound Recordz

H pound Recordz Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from H pound Recordz, Music Producer, Mangochi.

Machawi videos drops to day!!!....
16/08/2024

Machawi videos drops to day!!!....

Machawi Audio-video drops to day!!...

Machawi Audio-video drops to day!!...
16/08/2024

Machawi Audio-video drops to day!!...

31/01/2024

Recording Producer "Navigator" wa studio ya H Pound wati ali ndi masophenya okhala Dj Khaled wa ku Malawi popeza akuyamba kumamenyetsa macolabo ma artist omwe amaimba ku studio kwake.

Iyeyo wati chaka chino ayesesa kuti atulutse artist modzi ndipo azaimbe ndi Davido.

Padakali pano wati akutulutsa nyimbo yake yoyamba momwe muli GreazyMoh, Torey, Mits Wallan & Sixty Dada mu nyimbo yomwe mutu wake ndi "Phiko" Koman iye wati nyimbo zo ndzake koma iyeyo saziimba nawo.

Welcome Dj Khaled Navigator

Address

Mangochi

Telephone

+265885837767

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when H pound Recordz posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category