TDS MEDIA

TDS MEDIA Media team

18/01/2026

Tsiku la Sabata 🙏

Tsiku ngati la lero zaka zingapo zapitazo mmudzi mwa jwanthi m'boma la Kasungu  mudali chisangalalo chifukwa kudabadwa M...
11/01/2026

Tsiku ngati la lero zaka zingapo zapitazo mmudzi mwa jwanthi m'boma la Kasungu mudali chisangalalo chifukwa kudabadwa Mwana Wa mamuna m'banja la bambo Mvula.Iwo anamutcha Mwana wawo dzina nati uyu ndi khale Dokiso.

Lero Dokiso amadziwika ndi ntchito monga izi;mlerakhungwa,mtumbuka womasuka,odzichepesa,odzipereka ndi wolimbikira mu ntchito zambiri.

Managing director and staff members of TDS MEDIA ikukufunirani za bwino zonse pomwe mukusangalala tsiku lanu bwana Dokiso pitilizani kucheza bwino🥳🥳.

10/01/2026

Morning people

Happy birthday Asambazi...Nkhukumbirani viyemi vyonse🥳🥳🥳
09/01/2026

Happy birthday Asambazi...
Nkhukumbirani viyemi vyonse🥳🥳🥳

Sizinayende apapa 💔💔
09/01/2026

Sizinayende apapa 💔💔

09/01/2026

Kumayamika

08/01/2026
Zomwe timapanga nthawi ina zimakhala kuti zakhazika mutu.The more we do on our dream ena amakhala akuvesera mwachidwi ko...
08/01/2026

Zomwe timapanga nthawi ina zimakhala kuti zakhazika mutu.The more we do on our dream ena amakhala akuvesera mwachidwi koma safuna kutulukira poyera but yesterday, I was very surprised with what certain lady did.

Kungondiona ndikudusa pa chibungo trading centre wayamba kunenera mpira avekere
"wautenga Haulace kudzapatsira Maxwell kudzayesa kupereka chakumazere koma mpira kudzangotuluka akuti ikhale throw in"

I don't know how to thank her because this too is love.
The dream is flying higher we just pray for this.
May good lord help the dream to shine.

Sitingaphwekese am so happy mama🥰🫶🙏

TDS MEDIA
Breaking barriers bringing solutions

Address

Mangochi

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when TDS MEDIA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share