LAXAS MUSIC

LAXAS  MUSIC Welcome all, this is all about entertainment and music promotion

15/05/2025

ONa

16/04/2025

Kwakoma ndikuno

Apaso ndipena pomwe ife sitikumvesa
16/04/2025

Apaso ndipena pomwe ife sitikumvesa

Kuti zimveke bwanji?
16/04/2025

Kuti zimveke bwanji?

24/7 on this page now ,let's make it together
16/04/2025

24/7 on this page now ,let's make it together

02/01/2024
10/09/2023

NEW SHOW LOADING

Tayakisa
06/09/2021

Tayakisa

Get funny and like de Page
15/08/2021

Get funny and like de Page

09/08/2021

MACHEZA AKUMWAMBA

Jacob : kodi a Izeki kuchoka amachoka chochija?
Izek : hahaha. . .iwenso wabwerako. . . . iwe umaona ngat chani? ndi pa Malawi pamenepaja ase!
Jacob : eeeh patelera,nanji ndi COVID,akusosola anthu.
Bingu : paja inu mukakumana. . . musayambepotu apa,kuno kulibe zosekesana.
Kamuzu : kdi iwe Izek,mzako umamutchulatchula uja ndameneyu?
Izek : eya,kma eeeh. . . . akt ku Malawi kwanunkhatu!
Chilebwe : ndichaniso. . . . azungu aja ndinakabera mfuti ku Mandala aja ayambiranso zofoila zija?
Jacob : ayi,pano kuli Abusa Ndi amzake!
Kamuzu : nde utiso ameneyo?
Jacob : mkulu amene akulamulira Malawi ndi chipani chanu chija!
Kamuzu : sha! kdi,mpaka abusa mu MCP. . . . J tembo anatha eti? mpaka kulora kt abusa alamulire?
Matafale : Ekhaya! ekhaya!. . . nde abusa mpaka kupangisa kt pa ground patelere?. . . atcheya ali bhobo kma?
Jacob : alibwino,amangopereka moni!
Matafale : k*kk ok k*k paja ndinamulembera kalata ya 500 pages k*k
Bingu : Chala mwamba,kma ati ku DPP chinavuta ndi chani kt aluze?

Jacob: malawi anazindikila

Next?

Like the page

Address

Namphungo
Mulanje

Telephone

+265992589408

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when LAXAS MUSIC posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to LAXAS MUSIC:

Share