News-line Malawi

News-line Malawi Promoting media and equal access to viable informations

29/10/2023

Authorities at Reserve Bank of Malawi says for over a period of 3 to 4 years they have replaced banknotes with a value of 200 billion Kwacha.

Samuel Senzani Reserve Bank of Malawi Currency Operations Manager disclosed this in Nsanje on the sidelines of public engagement meetings central bank officials held in the district.

According to Senzani, the replacement of the damaged banknotes cost the central bank 20 billion Kwacha annually.

He cited throwing of cash during social gatherings such a weddings as some of malpractices leading to currency destruction in the country.

Senzani was however quick to disclose that following these public engagements there has been positive response on the part of members of public on proper use of currency to avoid destruction.

29/10/2023

A woman at a hospital in Khan Younis in the southern Gaza Strip embraces the body of a Palestinian child killed in Israeli strikes, October 17, 2023. 
 
Israel has put Gaza under a total siege and subjected it to intense bombardment. It has vowed to annihilate Hamas after the Islamist militant group killed 1,400 people and seized hostages in an Oct. 7 attack on Israel. The Gaza health ministry says Israeli air strikes have killed more than 3,000 since then.
 
🔗 Read the latest about the war at our link in bio. 📷

29/10/2023
29/10/2023

GRAIN Millers Association of Zimbabwe says its members have started to import maize to bolster national stocks ahead of the expected El Niño-induced drought.>https://tinyurl.com/ytw9pub8

29/10/2023

Katswiri ochita masewero a nkhonya Tyson Fury wagonjetsa katswiri wakale wa UFC Francis Ngannou wamdziko la Cameroon kudzera mu chiganizo cha oweruza (Judges split desicion) usiku wathawu mu mdziko la Saudi Arabia.

Aka kanali koyamba kuti awiriwa akumane mu nkhonya yomwe inali ya zigawo 10 (10 rounds) koma yosalimbirana lamba yemwe akusungira Tyson Fury wa WBC.

Ngakhale Ngannou kanali koyamba kuchita mpikisano wake wa nkhonya koma anakwanitsa kugwetsa Fury mugawo lachitatu, komanso kuchita bwino mzigawo zina kusiyana ndi zomwe anthu amayembekezera.

Komabe ngakhale Izi zidadzidzimutsa anthu ambili, Fury adachitabe bwino mzigawo zina zotsatira, mpaka kupeza chipambano kuchokera Ku chiganizo cha oweruza (Judges ) omwe amayang'anira nkhonya yi.
Arabia.

-Gift Mthunzi

29/10/2023
29/10/2023
29/10/2023
10/10/2023

Zadziwika kuti pofika usiku wa lolemba sabata ino anthu oposera 200 omwe adapita ku mwambo wa Mulhako wa Alhomwe kwa Chonde m'boma la Mulanje sanachoke kumalowa kubwelera ku makomo awo kaamba ka vuto la mayendedwe.

Mzati itafika kwa Chonde komwe kumachitikira mwambowu nthawi ya 9 koloko usiku omwe uno yapeza anthuwa ali kakasi kusowa mtengo ogwira.

Poyankhula ndi m'modzi wa anthu omwe tinawapeza ndipo wasankha kusatchulidwa dzina anati izi zachitika kaamba koti atsogoleri omwe amayendetsa mwambowu sadawapatse ndalama zoyendera.

Iye wati anthuwa akuvutika kwambiri maka pankhani ya chakudya, malo ogona komanso chitetezo.

Koma wapampando wa Mulhako wa Alhomwe mchigawo cha kumwera a Blessing Makwinja ati anthuwa anagobwera mopanda dongosolo loyenera la atsogoleri a Mulhako choncho sadawerengeledwe pa chikonzero cha ndalama za mayendedwe.

A Makwinja ati akuluakulu omwe amayendetsa mwambo wa chaka chino akuchita chothekera kuti anthuwa abwelere mmakwawo.

Ena mwa anthu omwe adakali ku malowa ndiwochokera ku Salima, Nkhotakota, Lilongwe ndipo ena mwa anthuwa ndi ophunzira pa sukulu ya Bunda.

Mwambo wa Mulhako wa Alhomwe wachaka chino unachitika kuyambira pa 6 mpaka pa 8 October Chaka chino kwa chonde ku Mulanje.

Wolemba: Chrispine Dzimbiri.

10/10/2023
09/10/2023

News

Apolisi ku Lilongwe apeza galimoto lobedwa ndikumanga anthu awiri omwe akuganiziridwa kuti adapha mwiniwake ndikuponda mtembo ndi galimotoli kuti iwoneke ngati ngozi.

Apolisi agwira awiriwa akusasa galimotoli, lomwe ndi la mtundu wa Probox, pamtengo wa K1.5 million ku msika wa Malangalanga kuti ena ayiphwasule n'kumagulitsa zipangizo chabe (spare parts).

Mneneri wa polisi ya Lilongwe a Hastings Chigalu wati a Kondwani Kampala a zaka 25, omwe anali ndi a Charles Mapemba a zaka 35, adapeza a Friday Ganizani nkuwapusitsa kuti akufuna kupanga hayala.

Iwo akuganiziridwa kuti atafika pa Nalikule usiku wa Lamulungu adapha mwini galimotoyi, n'kuponda mtembo ndi galimoto loberedwalo.

A Chigalu ati apolisi anagwiritsa ntchito ukadaulo wawo kufufuza ndikugwira abambo awiriwa

Source Nations

Address

Chikonde
Mwanza

Telephone

+265991176894

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when News-line Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to News-line Malawi:

Share