Kukaya Nkhu Mpoto

Kukaya Nkhu Mpoto Tili bene na bene

YANKHANI NGATI MUPHUZITSI🖋️🖊️📚
01/08/2025

YANKHANI NGATI MUPHUZITSI🖋️🖊️📚

  Nkhu MpotoMtsogoleri wachipani cha Odya Zake Alibe Mlandu, Dr. Micheal Usi, wati mavuto omwe aMalawi akukumana nawo m'...
31/07/2025

Nkhu Mpoto

Mtsogoleri wachipani cha Odya Zake Alibe Mlandu, Dr. Micheal Usi, wati mavuto omwe aMalawi akukumana nawo m'dziko muno ndi kaamba ka dyera komanso kusakhulupirika kwa atsogoleri andale.

Dr. Usi ati mwachitsanso, atsogoleri andale ochuluka amangodziwa kulonjeza koma osakwaniritsa, zomwe zimachititsa kuti anthu m'dziko muno adzikhalabe pa umphawi wadzawoneni.

Iwo alankhula izi pasitolo za Suza m'boma la Kasungu komwe anachititsa misonkhano wa ndale, komwe amema anthu kuti adzawavotere, pofuna kuti zinthu zisinthe m'dziko muno.

Dr. Usi womwenso ndi wachiwiri kwa m'tsogoleri wa dziko lino, anapereka chitsanzo chakupitirira kusowa kwa mafuta agalimoto, ponena kuti adindo akungodziwa kulonjeza koma osathetsa vutoli.

Mfumu yayikulu Suza ya m'boma la Kasungu, yati njala yafika posawutsa kwambiri m'dera lake, ndipo yapempha adindo kuti achitepo kanthu mwansanga.

(by Kukaya Nkhu Mpoto-Dowa: 07/31/25)

18/07/2025

Timanyane kukaya nikochi...?

Chakukaya🤣
18/06/2025

Chakukaya🤣



Nafuma.Navileka.

Nduna yakulaŵiska vya malonda a Vitumbiko Mumba ŵalangula kuti ŵafuma mu komiti yikulu ya chipani cha Malawi Congress (MCP).

Pakuyowoya na Zodiak iwo ŵati ŵachita ntheula chifukwa cha kuvuka na ndyale za vidimbiko, ndyale zakuphakana malikho na mautatavu.

Kuyana na ŵa Mumba, ŵalongozgi ŵanyakhe ŵatatu mu MCP ŵakutora chipani nge ntchawo.

Ivi ndivyo vyaŵachiska kuwezga buleki pakuti wakukhumba yayi uchitiro wakuyuyulana na kwendelana mphiska ngani Yuda Esikarioti.

Iwo ŵati mtima wawo waraŵiska mphinjika ya chisola cha mwimiliri wa mphara ya malango wakurwande la pakati mu boma la Mzimba.Iwo kwene ŵati ŵachali membala wa MCP.

(by Dickson Chivwati Gondwe-Lilongwe:06/17/25)

16/06/2025
wasolokela😂
25/04/2025

wasolokela😂

04/03/2025

Wakukaya let's gather here and confuse achewa,
Walya nthimphwa🙊

28/02/2025

MWAUKA ULI MWAWANYANE PANO!?
TIONE K*T WAKUMUPOTO NDAN!?

08/01/2025

HOW TO MAKE YOUR OWN QUALITY POULTRY FEED.

As a Farmers, you can create your own poultry feed using the Pearson Square method. This method helps ensure that the feed contains the right amount of digestible crude protein (DCP), which is essential for the nutrition of chickens.

Here’s how you can do it:

Ingredients and Their DCP Values:
- Whole maize: 8.23%
- Soya: 45%
- Fishmeal (omena): 55%
- Maize bran: 7%
- Sunflower: 35%

For example, if you want to make feed for laying hens (layers), the feed should have at least 18% crude protein.

Making a 70kg Bag of Feed for Layers:
To make a 70kg bag of feed with 18% crude protein, you need:
- 34kg of whole maize
- 12kg of soya
- 8kg of fishmeal (omena)
- 10kg of maize bran
- 6kg of lime (as a calcium source)

Calculating Crude Protein:
To check if the feed meets the 18% protein requirement, do the following calculations:
- Whole maize: 34kg × 8.23 ÷ 100 = 2.80%
- Soya: 12kg × 45 ÷ 100 = 5.40%
- Fishmeal: 8kg × 55 ÷ 100 = 4.40%
- Lime: 6kg × 0 ÷ 100 = 0.00%

Total crude protein = 2.80% + 5.40% + 4.40% = 12.60%

To get the total crude protein percentage in the 70kg bag:
12.60% ÷ 70kg × 100 = 18%

So, the feed has 18% crude protein, which is perfect for layers.

Ready-Made Formulations:
To make it even easier, here are ready-made feed formulations for different stages of chicken growth:

Chick Mash (1-4 weeks)
Ingredients for a 70kg bag:
- 31.5kg whole maize
- 9.1kg wheat bran
- 7.0kg wheat pollard
- 16.8kg sunflower or linseed
- 1.5kg fishmeal
- 1.75kg lime
- 30g salt
- 20g premix amino acids
- 70g tryptophan
- 3.0g lysine
- 10g methionine
- 70g threonine
- 50g enzymes
- 60g coccidiostat
- 50g toxin binder

Growers Mash (4-8 weeks)
Ingredients for a 70kg bag:
- 10kg whole maize
- 17kg maize germ
- 13kg wheat pollard
- 10kg wheat bran
- 6kg cotton seed cake
- 5kg sunflower cake
- 3.4kg soya meal
- 2.07kg lime
- 700g bone meal
- 3kg fishmeal
- 14g salt
- 1g coccidiostat
- 18g pre-mix
- 1g zinc bacitracitrach
- 7g mycotoxin

07/01/2025

TODAY'S FIXTURES (TUE, JAN 7)
(1st Leg)
Arsenal vs Newcastle 10:00 pm

Sporting CP vs FC Porto 9:45 pm

Al-Taawon vs Al-Qadisiya 5 pm
Al-Hilal vs Al-Ittihad 7:30 pm

Club Brugge vs Leuven 9:45 pm
St Truiden vs Gent 9:45 pm

Eldense vs Valencia 10:00 pm

YESTERDAY'S RESULTS (JAN 6)

Inter Milan 2-3 AC Milan

Wolves 0-3 Nottingham

D.Minera 0-5 Real Madrid

QPR 2-1 Luton Town

Gil Vicente 1-1 Rio Ave

Al-Raed 1-1 Al-Jabalain (Pen 4-3)
Al-Shabab 2-1 Al-Feiha

RB Salzburg 0-6 Bayern Munich
RB Leipzig 10-0 Banik Most-Sous
Dusseldorf 0-1 Feyenoord
Hoffenheim 3-1 Augsburg

Koma ku Silver Strikers FC  uku kuli zimimba🤣🤣🤣 anyway mmakwana ma champions athu 🏆🏆
07/01/2025

Koma ku Silver Strikers FC uku kuli zimimba🤣🤣🤣 anyway mmakwana ma champions athu 🏆🏆

Tengani onse basi
28/12/2024

Tengani onse basi

Address

Mzimba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kukaya Nkhu Mpoto posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share