Golden City Tower

Golden City Tower Golden City Tower is a media and entertainment company
(6)

A Royal Image ndi Kwenda.co alengeza kuti anthu  omwe anagula matikiti onse 824 a Standard ndi VIP abwezeredwa ndalama k...
10/01/2026

A Royal Image ndi Kwenda.co alengeza kuti anthu omwe anagula matikiti onse 824 a Standard ndi VIP abwezeredwa ndalama kutsatira kuyimisidwa kwa The Hive Experience 2025.

Chiwonetserochi chinayimisidwa chifukwa cha imfa ya mamembala asanu a Hive Band pa ngozi.

Omwe sanalandire ndalama awo alumikizane ndi:
📧 [email protected] / [email protected]

👉 Titsatireni pa WhatsApp channel yathu kuti mupeze nkhani zambiri:
https://whatsapp.com/channel/0029Va9FLXf0bIdjdvHzFy1x

NKHANI YACHISONI 💔Wapolisi wina wa ku Mtakataka Police Station, Detective Sub-Inspector Lawison, wamwalira atamenyedwa n...
10/01/2026

NKHANI YACHISONI 💔

Wapolisi wina wa ku Mtakataka Police Station, Detective Sub-Inspector Lawison, wamwalira atamenyedwa ndi anthu okwiya ku Tchanga Irrigation Scheme ku Dedza East.

Malingana ndi apolisi, Lawison ndi mnzake anapita kuderalo kukamanga munthu woganiziridwa kuti anaba mbuzi. Munthuyo atathawa, Lawison anawombera mfuti yachenjezo koma munthuyo sanayime. Mfutiyo idalakwika kugunda munthu wina amene ankadutsa ndipo adamwalira pomwepo.

Izi zinakwiyitsa anthu am’mudzimo omwe anayamba kuthamangitsa apolisi awiriwo. Lawison adamangidwa, kumenyedwa ndi kuponyeredwa miyala mpaka kumwalira.

Mnzake wapolisiyo wavulala kwambiri ndipo akulandira chithandizo kuchipatala cha Mtakataka.

Kisah  LoyalThe story of loyalty, coming to life. 🎬🔥Video dropping soon
10/01/2026

Kisah Loyal
The story of loyalty, coming to life. 🎬🔥
Video dropping soon

09/01/2026

⚽FULL TIME ⚽

Cameroon 0 : 2 Morocco

09/01/2026

Cameroon 0 : 2 Morocco

09/01/2026

Cameroon 0 : 1 Morocco) 25mins

Uwu ufunga⚽⚽⚽

Apolice mundimangiranji ine, Popanda G***a ine sinditha...
09/01/2026

Apolice mundimangiranji ine, Popanda G***a ine sinditha...

Tizikhala Serious
09/01/2026

Tizikhala Serious

Ishan Cyapital nayeso wakozekatu kuphulisa mabomba chaka chino...New Year New Sound.
09/01/2026

Ishan Cyapital nayeso wakozekatu kuphulisa mabomba chaka chino...

New Year New Sound.

Address

Box 20664 Mzuzu
Mzuzu

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Golden City Tower posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Golden City Tower:

Share