News roum

News roum Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from News roum, Media/News Company, Mzuzu, nkhata Bay, chikwina, Mzuzu.

09/02/2021

Gys, zikoli likuwoneka ngatikuti likupita kumapeto chifukwa zonse zinalonjezedwa mu Bible zakwanilisidwa, anzanga mukuwonabwa bwa?

Yesu anati ufumu wakumwamba ndiwana, akutanthawuzanji kwa ife?
09/02/2020

Yesu anati ufumu wakumwamba ndiwana, akutanthawuzanji kwa ife?

09/02/2020

Ngodala amlakalaka kumva mau amulungu nthawi zonse, pakuti muli chipulumuso

29/09/2019

Oh guys, Mon ,Mon mafans

09/09/2019

Anzanga, Kodi nkhani yama Er****on yilipati ku court sopano? Ndikonda kumvera Zbs nawoso angoti ziii osamvekaso.

Ine ndi mwana wangayu ndikusowa mau achilimbikiso a uzimu, ndithandizen abale
07/09/2019

Ine ndi mwana wangayu ndikusowa mau achilimbikiso a uzimu, ndithandizen abale

07/09/2019

1john 1:1-- - - likut pachiyambi kunali mau, mawuwo anali kwamulungu, ndipo mawuwo ndiwo mulungu. Ine sindikuvesa bwinob kutambasula kwake, ndithandizeni

Address

Mzuzu, Nkhata Bay, Chikwina
Mzuzu

Telephone

+265991881912

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when News roum posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share