Malawi na Zambia

Malawi na Zambia Kuchimake kwa Nkhani Zochitika ku Malawi na Zambia mosatengela mbali, Palibe Kubisa kapena Kupsatira.

26/08/2025

Zoti kudali matenda a mphutsi ana ama 2pin sangaziziwe. Anthu okonda kupakula mumakumana nazo hhmm..

Mahop achigulu
23/08/2025

Mahop achigulu

Paja makolo amzako samakhala akulu.
18/08/2025

Paja makolo amzako samakhala akulu.

Anthu amene akubhebhesa pa Malawi pano. Eeh.. adyana, eeh.. adya ndalama eeh... Chipwilikiti. Side note: Don't marry.
15/08/2025

Anthu amene akubhebhesa pa Malawi pano. Eeh.. adyana, eeh.. adya ndalama eeh... Chipwilikiti.

Side note: Don't marry.

Alikuti Zeliwe Waku Zokonda Amayi? Anasiya kupeleka ma cross mmhh..Mwinatu account yake idapangidwa hack. Those who are ...
14/08/2025

Alikuti Zeliwe Waku Zokonda Amayi? Anasiya kupeleka ma cross mmhh..Mwinatu account yake idapangidwa hack. Those who are close to her, check up on her mwina akudusa munyengo zowawatu.

Manganya iwe why?😭😭😭💔
13/08/2025

Manganya iwe why?😭😭😭💔

Why is he trending?Tianthu tifupi tifupi sitimakhala ndi mantha hhmm..
13/08/2025

Why is he trending?
Tianthu tifupi tifupi sitimakhala ndi mantha hhmm..

Komatu Dorothy mwendowo nde kuwupaka komba. Anthu atutumuka ndi mwendo onona. Uyu agwesa anthu mmayeselo.
13/08/2025

Komatu Dorothy mwendowo nde kuwupaka komba. Anthu atutumuka ndi mwendo onona. Uyu agwesa anthu mmayeselo.

13/08/2025

Komano Bakili Muluzi TV si mfiti?🤔🙌

Nde chikazati "HOW FAR DID YOU GO WITH YOUR EDUCATION?". Amene adalibe phone musayankhile.
13/08/2025

Nde chikazati "HOW FAR DID YOU GO WITH YOUR EDUCATION?". Amene adalibe phone musayankhile.

Odya zake alibe mulandu. Uyu ayimaliza MCP.
13/08/2025

Odya zake alibe mulandu. Uyu ayimaliza MCP.

Banja ndi lomweli sitikusintha. Leah Malekano and bae. Achokatu kutali. Si oyimba anu aja ongokumana ma memory card odza...
12/08/2025

Banja ndi lomweli sitikusintha. Leah Malekano and bae. Achokatu kutali.

Si oyimba anu aja ongokumana ma memory card odzadza ndi nyimbo kale kumakanika kuyikamo ina.

Address

Luwinga
Mzuzu

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi na Zambia posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Malawi na Zambia:

Share