19/08/2026
1 Akorinto 10 v 12.
Choncho,ngati mukuganiza kuti mwayima mwamphwnvu,samalani mungagwe.
Ana a Mulungu tiyeni tikhale osamala popedza timaona ngati chifukwa ndife oimbira ,otumikila tilinawo maudindo ku church ndife amphanvu ku moyo wauzimu koma zindikilani pamene ukuona ngati waima mwa mphanvu samalani mungagwe.Mulungu atithandize kukomza moyo wathu kumagawo onse isanafike nthawi yotaya chipulumutso .