God Plus News Update

God Plus News Update Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from God Plus News Update, Media/News Company, Blantyre, Ndirande.

Ife a gord plus news update tikukuziwisani kt tili ndi mpikisano omwe uzichitika tsiku lilironse kwa masabata anayi ndip...
14/09/2022

Ife a gord plus news update tikukuziwisani kt tili ndi mpikisano omwe uzichitika tsiku lilironse kwa masabata anayi ndipo chofunika kuchita pangani like page yathu madzulo tiponya mafutso ndipo yemwe ayakhe molondola azilandira ma units okwana 1500

12/09/2022

Morning people

22/07/2022

Kwa amene mukufuna group lapa whatsapp la god plus news update ndipangeni hy ku whatsapp pa

0980219891

21/07/2022


Super League Fixtures

--DigiSports
_23 July 2022_
🔖Nyasa Big Bullets🆚Kamuzu Barracks@Kamuzu🏟️
⏰14:30
(Capital City Derby)
🔖Silver Strikers 🆚 Civil Service United@Silver🏟️
⏰14:30
🔖Moyale Barracks🆚 WakaWakaTigers@Mzuzu🏟️
⏰14:30
-DigiSports
_24July 2022_
🔖Sable Farming🆚Dedza Dynamos@Mulanje Park🏟️
⏰14:30
🔖Rumphi United 🆚 Ekwendeni Hammers@Rumphi🏟️
⏰14:30
🔖TN Stars🆚 Mighty Mukuru Wanderers@Kasungu
⏰14:30
🔖Karonga United🆚 Blue Eagles@Karonga🏟️
⏰14:30
🔖Civil Service United🆚Red Lions@TBA🏟️
⏰14:30



*MTSOGOLERI* *WADZIKO LA* *KENYA WASISA* *MITENGO*  Mtsogoleri wadziko la Kenya  Uhuru Kenyata wasisa kwambili zedi mite...
21/07/2022

*MTSOGOLERI* *WADZIKO LA* *KENYA WASISA* *MITENGO*

Mtsogoleri wadziko la Kenya Uhuru Kenyata wasisa kwambili zedi mitengo yachimanga, mafuta agalimoto ndizinthu zina.

Kenyata wasisa mtengo wamafuta agalimoto kuchoka pa Ksh209.95 kufika pa Ksh 159.12

Mtengo wamagetsi wasisa ndi 15%

Ufa wachoka pa Ksh210 kufika pa Ksh100

Zonsezi zikuchitika pomwe mtsogoleri wadziko lino Dr Lazarus Chakwera ndiboma lake akuchitila nkhanza a Malawi pomakweza mitengo mwachisawawa.
MEANWHILE
President wa ku Zambia walemba aphunzitsi 33000 mu chaka chimodzi, pomwe president wa dziko linalake wayankhula chizungu chabwino kwa zaka ziwiri ndi miyezi ingapo.

Bungwe la CDEDI lati lakonza ziwonetsero zofuna kukakamiza mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera kupungulako mph...
21/07/2022

Bungwe la CDEDI lati lakonza ziwonetsero zofuna kukakamiza mtsogoleri wa dziko lino, Dr Lazarus Chakwera kupungulako mphamvu zake apo biii atule pansi udindo.

CDEDI yati a Chakwera ndi boma lawo achite chilichonse chothekera kuti asinthe gawo 91 la malamulo a dziko lino ngati akufuna kukhalabe pa chiwongolero.

Mtsogoleri wa CDEDI, Sylvester Namiwa wati zokonzekera zonse za ziwonetsero zokakamiza a Chakwera kutula pansi udindo zili mchimake ndipo sakuchitanso zopambapamba.

Address

Blantyre
Ndirande

Telephone

+265980219891

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when God Plus News Update posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share