18/08/2025
Dr. Bingu Wa M***arika came to power through UDF, koma atawona vision yawo, anawona kuti ku UDF sangakwanitse kuzikwaniritsa and so, he had to go elsewhere where his vision and institution blend with the vision and for Bingu, anayambitsa DPP, yomwe anayipatsa culture yomwe iwowo ankayifuna.
Dr. Saulos Chilima anayambira ndale zawo ku DPP, koma later anawonanso kuti masomphenya maka othetsa katangale, tsankho lamitundu, ma reforms, sizingatheke pansi pa DPP, he moved on to form UTM.
Ine ndinayambira ndale ku DPP, tinayesayesa koma tinawona kuti ayi tisunthe. Sindinangofikira kulowa UTM, ndinayang'ana zipani zambiri, their mission statement, culture and values, ndipo ndinawona strong desire from UTM to end corruption, nepotism, reform government system, bring innovation and develop Malawi, I was convinced UTM is the right place to be.
Ndikunena ichichi ambiri timatsatira zipani mchimbulimbuli, kuwafunsa kuti awa mmawasapota chifukwa chani, munthu wa degree, masters or PhD imene amakanika kuyankha, chomwe angakuwuzeni nkuti ngwa ku Ntchisi, Dowa, Mulanje, Thyolo, Rumphi, Karonga. So, ophunzira ndi osaphunzira osasiyana.
I want to challenge everyone here, politics is life, kuchipatala kulibe mankhwala a TB, ma patient a TB ngati sakulandira mankhwala next thing ndi imfa, imfayo sisankha kuti awa ngakudedza musawaphe, iphani aku Phalombe, tonse tifa. Njala siwona Mchewa kapena Mtumbuka, imapha aliyense chimodzimodzi ilibe tsankho
Tiyambe kuwona ndale in line with our lives komanso dziko. Tikupindula chani, dziko likuyenda bwanji, titsatire chipani chomwe chili nkuthekera kofewetsa miyoyo yathu komanso kutukula dziko lathu.
Amati, you can't get different results by doing same things that failed. Pangani chisankho chopanga join this movement, for the sake of Malawi. Our country is bleeding, anthu akufa muzipatala, 65% ya imfa zathu timafa because of failed health systems. Abale athu ambiri analowa mmanda osati nthawi inakwana, koma tinalephera kuwasamala. UTM i