Neno wathu

Neno wathu Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Neno wathu, Digital creator, Neno, Neno.

02/04/2024

Anyamata aku Neno odolo sikuba....ndizochititsa manyazi munthu mpaka kufika pokuba mutu wa nkhumba oti umafuna udyedwe ku turn up....tiyeni tisinthe ndi umbuli otheratu omwe unachitidwa apawu

02/04/2024

For the first time ku Neno kuchitika turn up ma report akuwonetsa kuti zinali bwino anthu akufuna zipitilire...big up kwama guy omwe munapanga organize everything 🔥🔥🔥

25/08/2023

Atalenga dziko lapansi MULUNGU
anadzalengaso ku NENO.......nkokomatu 🔥🔥🔥

25/06/2023

Mukhale ndi tsiku lopambana nonse 💞

23/06/2023

Good Morning anzanga nonse aku NENO...? 😁

30/04/2023

You get what you focus on, so focus on what you want

Good morning 🌄

28/04/2023

Monga mene tinanenera matsiku am'mbuyomo kuti tizikhala tikuthandiza anthu ochepekedwa munjira zosiyanasiyana. Lero tafuna kukuziwitsani kuti tikufuna ana amene amavutika kumbali yamaperekedwe a school fees. Tikufuna ana okwana four (4).
Akhale ophunzira apa Chiwale Day Secondary School awiri(m'nyamata m'modzi komanso mtsikana m'modzi)

Komanso ophunzira apa Chikonde Community Day Secondary School awiri (m'nyamata m'modzi ndi mtsikana m'modzi)...
Ngati alipo oti mukuwaziwa kuti amavutika maperekedwe a fees, tipezeni ku inbox ndipo mutipase maina awo

Zikomo....

27/04/2023

"If you want to put a smile on God's face today, put a smile on somebody else's face, "

Good morning fam ❤

26/04/2023

Kumbukirani kuti Pemphero limatisintha ifeyo koma chikhulupiliro chimasintha zinthu. Osamataya chikhulupiliro

Good morning fam ❤

25/04/2023

Usiku wabwino. Osaiwala kupemphera 🙏

25/04/2023

Good morning fam ❤

10/02/2023

Hello people 📢 👨‍👨‍👦
Tapangeni invite anzanu kupanga like page yathuyi by sharing them this post.....anthu 10 oyambirilira kupanga comment and share post imeneyi alandira ma units okwana k200.Tumizani screenshot yanu kutionesa anthu omwe mwapanga invite ndipo pompo pompo mulandira mpoto yanu...zikomo 🙏🙏🙏

Address

Neno
Neno

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Neno wathu posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share