18/01/2024
CHINTHU CHOOPSA CHICHITIKA POSACHEDWAPA
Posachedwapa kuchitika chinthu chimene chiyimitse mitu mafumu,olemera,osauka,otchuka
Palibe amene amvetsetse chifukwa chichitika mosayembekezera
Chinthu chimenecho chipangitsa anthu kusaka mawu a Mulungu
Chipangitsa anthu kusiya kutsutsa kapena kunyoza mawu a Mulungu
Chipangitsa anthu kusiya kupemphela mwachibwana
Chipangitsa anthu olemera kusiya chuma ndikunthamangira zauzimu
Chipangitsa anthu kumadzipha okha koma osafa
Chinthu chimenecho chipangitsa azimayi kusiya kumvala ma Trauza,kuphoda, kumvala gogoda,kumanga Meshi
Chinthu chimenecho chipangitsa anthu kusiya kumvala makabula,tothina, kumeta mbali mbali, kumvala jeas,kuonera zalaura,mpira, mwano,dzigololo,kuba,kusuta,kupembedza mayi mariy
Dziko lonse likhudzika, dziko lonse likhala pachisoni, dziko lonse likhala pamaliro osantha koma zikhala zopanda tchito
Mateyu 24:40
Pomwepo adzakhala awiri m'munda; mmodzi adzatengedwa, ndi wina adzasiyidwa
Chinthu chimene chikunenedwa apachi ndi MKWATULO
M'bale mkwatulo uchitike posachedwapa kudzatenga oyera mtima lero,mawa, nthawi inayiliyonse
Udzalira mowo wako onse ukadzatsala pa mkwatulo
Untha kuchita chibwana lero ndikumati ndidzalapabe koma ukadzatsala sudzaupeza mwai
Udzauda mowo wako onse sudzaukondaso Mpaka kugahena wamoto
CHISOMO CHIDAKALIPO LERO UNTHA KUKOZA MOYO WAKO, UNTHA KUMULANDILA YESU LERO CHIFUKWA MKWATULO UKAPITA PALIBE KUKHULULUKIDWA LAPANI LAPANI LAPANI ..
Ngati mukufuna mudzimva mawu a Mulungu pangani zinthu ziwiri izi
1.Ndinani mawu awa Mawu a Mulungu Omwe akuoneka poyambilirawo
2.ndipo mukatsekula ndinani kadzanja kamene mukaoneko
Chonde tumizirani azanu komaso m'magrup omwe muli uthengau kuti nawoso awerenge nawo
Muntha kulowa ku group lanthu podina mawu awa
UTHENGA WA MASIKU OTSILIZA GROUP
Ambuye Akudalitseni mochuluka
Wolemba: MOVISH MADISHUH phalombe