Mpisa wa Mpisa My Vote- PE North East

Mpisa wa Mpisa My Vote- PE North East Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Mpisa wa Mpisa My Vote- PE North East, Box 96 , Phalombe, Phalombe.

Hon. Wilfred Mpisa akufunira zabwino zonse anakubala onse mdziko muno.
15/10/2025

Hon. Wilfred Mpisa akufunira zabwino zonse anakubala onse mdziko muno.

02/10/2025

Pamene Tikudikila kulumbilisidwa Hon Wilfred Mpisa wasimikizila anthu a dela lake kwa T/A Kaduya, Maoni komaso Chiwalo kuti sakudikilaso ayi koma ntchito iyambike ..moti tikunena pano mijingo ikukumbidwa komaso ma tractor ali pa ground kupala miseu yonse mudelari ngakhale iwo sanalumbire..

Hon Wilfred Mpisa amayakhula izi kwa antolankhani ku Blantyre podabwa ndi mavote ochuluka omwe iwo apeza kuchokera kwa anthu a Phalombe North East.

01/10/2025

It's now official MEC declared Wilfred Mpisa MP for Phalombe North East

With lovely heart we thank all people of Phalombe North East for the trust you have kwa Wilfred Mpisa tikuti zikomo

We are assuring you people of Phalombe North East (Swang'oma and Mauzi Ward) that we will prioritise your needs, focusing on development projects that benefit the entire community.

Wilfred Mpisa's agenda development is a collective responsibility, requiring collaboration with stakeholders and pledged to allow these stakeholders to operate without interference and motivate those working towards the constituency's development agenda

Wilfred Mpisa believes that even those who didn't vote for Mpisa on September 16 should not be hindered on service delivery.......Lastly let's give a big credit to our former MP Dennis biscuit Namachekecha for the foundation he laid for past 11 years . For the progress Wilfred Mpisa will start from Where Our former MP left for the betterment of our constituency

Akuti tili mugulu la aphungu omwe tatipula kwambiri kuposa onse.
26/09/2025

Akuti tili mugulu la aphungu omwe tatipula kwambiri kuposa onse.

From the office of Phalombe North East Member of Parliament Elect ..Wilfred Mpisa
25/09/2025

From the office of Phalombe North East Member of Parliament Elect ..Wilfred Mpisa

Zikomo abale nonse a Phalombe North East Consultancy pokhulupira Wilfred Mpisa kuti akhale MP wanu kwa zaka 5 zikubwelaz...
24/09/2025

Zikomo abale nonse a Phalombe North East Consultancy pokhulupira Wilfred Mpisa kuti akhale MP wanu kwa zaka 5 zikubwelazi. Pa anthu 28,154 omwe anaponya vote, anthu 20,143 mwasankha Wilfred Mpisa pakati pa anthu 7 omwe amapikisana. Ndipo anthu 33,060 mwavotera aDad Professor Arthur Peter Mutharika ngat President.

Tikulonjezani kuti sitizakukhumudwisani ndipo tiyeni tigwire ntchito limodzi.

Zikomo zikomo Zikomo




KUCHOKERA KWA HON. DENNIS NAMACHEKECHAThis morning, I reached out to congratulate my brother, MP-Elect Mr. Wilfred Mpisa...
17/09/2025

KUCHOKERA KWA HON. DENNIS NAMACHEKECHA

This morning, I reached out to congratulate my brother, MP-Elect Mr. Wilfred Mpisa, for the spirited campaign he has run. I wished him strength, wisdom, and success as he carries forward the hopes of our people in Swang'oma and Mauzi wards.

In his reply, he assured me of his respect and expressed his desire for us to work together for the betterment of our constituency.

This is the spirit that should guide us all, unity, mutual respect, and a commitment to serve our people. Leadership is not about division, but about joining hands to advance the common good.

Together, we can make Phalombe North East a better place for everyone.

𝐇𝐨𝐧. 𝐄𝐦𝐮𝐡𝐢𝐲𝐞 𝐃𝐞𝐧𝐧𝐢𝐬 𝐁𝐢𝐬𝐜𝐮𝐢𝐭 𝐍𝐚𝐦𝐚𝐜𝐡𝐞𝐤𝐞𝐜𝐡𝐚 𝐏𝐡𝐢𝐫𝐢
𝐅𝐨𝐫𝐦𝐞𝐫 𝐌𝐏, 𝐏𝐡𝐚𝐥𝐨𝐦𝐛𝐞 𝐍𝐨𝐫𝐭𝐡 𝐄𝐚𝐬𝐭.

17/09/2025
Zilikotu! Zilikooo! Koma Neba ulimbaaaaa?
13/09/2025

Zilikotu! Zilikooo! Koma Neba ulimbaaaaa?

13/09/2025

Dzuro pa 12 September 2025 titafika pa Migowi Post Office, Group Village Head Kaduya adapepha nkhani yamiseu pachifukwa choti nthawi zonse atsongoleri omwe analipo alephera ndipo apepha Wilfred Mpisa kuti miseu ikhale patsongolo komaso kukonza vuto lachakudya.

Mmau ake Wilfred Mpisa wawasimikizila anthu kuti iyi ndi mfundo yake yoyambilira pa zomwe azachite kuyambila lachitatu lino.

Pomaliza mfumu kaduya idapepha Wilfred Mpisa kuti azalimbikise pa nkhani ya maphunziro a Mmera mpoyamba kudela lake.

Anthu adali osangalala powaona aWilfred Mpisa akusitsa mfundo patsikuli ndi alonjeza kuti voti yawo la Chiwiri lino akapeleka kwa Wilfred Mpisa adpp komaso Peter Muthalika wa dpp

vote mpisa





Address

Box 96 , Phalombe
Phalombe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mpisa wa Mpisa My Vote- PE North East posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share