19/01/2025
NKHANI YONVETSA CHISONI YOMWE INA NDICHITIKIRA ANANDILUMIKIZITSA KUZIDOLO KOMA M'MATSENGA.
Dzina langa ndi innocent saona
Kungoyambira pachinyamata changa, moyo wanga wakhala osanvetsetseka malingana ndizomwe ndakhala ndikukumana nazo.
Ndimati ndikapeza kachibwezi, sindimatha chaka chisanathepo koma ine osalakwa.
Nthawi zambiri ndimakhala ndikukhumudwitsidwa koma vuto langa osalipeza.
Mpaka ndinafika pongo giver basi k*ti mwina zazibwezi simbali yathu. Zinalibe zovuta pauchinyamata kukhala opanda wachikondi.
Ma friends ndi anthu ena okuzungulira nkhani imakhala yanga Komabe nanga ndidakatani popeza ndimakhalira kukhumudwitsidwa.
Ndinakula mpaka 30 years koma opanda mkazi. Ndinakhala pafupifupi kwazaka 5 osaipeza ntchito.
Chirichonse sichimandiyendera ndipo ndimangosowa mtendere ndikamakhala nkumazifusa k*ti kwenikweni ine vuto ndichani?
Ndinapeza ntchito mwamwayi yomasesa komanso kukolopa ku restaurant ndipo ndinalidi ozipereka ndipo ndimailemekeza ntchito yanga. Ngakhale ndinali okhulupirika koma salary yanga samandikwezera pamene ena amawakwezera.
Pena mpaka ndimatha myezi iwiri osalandira, moti ndimalephera kungoisiya ntchitoyo k*ti nanga ndikaisiya ndilowera k*tiko???
Tsiku lina ndikusesa ndinaona munthu wina wabambo atakhala pa mpando akundikodola. Bamboyo amandiitanira chakudya k*ti tidye limodzi. Ndinayesesa kukana koma anakakamira ndithu mpaka ndinayambadi kudya naye.
Koma tirinkati mokudya muja, adandilakhula nk*ti chifukwa chani ndikuoneka osowa mtendere ndiwankhawa? Ine misozi inayamba kugwa ๐ญ๐ญ๐ญ ndikuchita kusowa poyamba kuyakhira.
Ndirinkati mozinvera chisoni muja, bamboyo adangondiuza k*ti lero ndikaweruka kuntchito ndingopita direct kunyumba kwanga ndipo ndizikapephera mpaka nthawi yoti ndigone ikakwane.
Atangolakhula choncho bamboyo adachokapo ndipo sindithaso kumuona komwe adalowera. Nthawi yowerukira itakwana, ndinayendadi direct wapakhomo panga.
Nditafika ndinayambadi kupephera mosweka mtima poona nyengo zowawitsa zomwe ndimadutsamo. Koma zoopsa ndithu zomwe ndidaziona ndiri nkati mopephera.
Ndidangonva chithu phiii kumbuyo kwanga, pompo ndidaimirira ndikuyang'ana. Ndinaonapo zidole ziwiri zitamangidwa ndi chanet cha green.
Pompo mtima wanga udachita mantha, koma ndirinkati mochita mantha momwemo, ndidanva kulakhula pa mtima panga k*ti usaope ndipo tenga lezala udule chingwe cha net cho.
Pompo ndinatenga lezala lija ndikudula, ndinazitenga zidolezo ndichingwecho kukazitaiya nchumbudzi. M'ma k*tacha ndinakonzeka bwinobwino ulendo waku ntchito.
Nditafika ndingoitaniridwa ku office ya abwana k*ti akundifuna.
Nditafikako ndinali odabwa abwana anga akundipepesa pazonse akhala akundilakwira ngati kusandipatsa malipiro anga. Adawerenga salary yanga yonse yomwe akhala asakundipatsa ndipo idakwana Mwk250,000. Pompo andandionjezerapo Mwk500,000 ngati chipepeso yonse kukhala ngati Mwk750,000. Ntchito adandikwezanso nandipanga kukhala oyang'anira ogwira ntchito onse pa restaurant po komanso adali ndikampani ina yomwe adandinyemerakonso kaudindo.
Anandipasanso nyumba yoti ndizikhaliramo.
Ndidamuona Mulungu akukhala kumbali yanga ndipo ndidakumbukira nkulu amene adandithandiza nzeru k*ti Mulungu yekha amutsogolele.
M'bale nk*theka nawenso nyengo zako pano ziri pa zero. Wakhala ukuyang'ana ntchito ndipo sukuipeza, wakhala ukuyang'ana mwamuna/mkazi wa serious koma nthawi zonse umangokhala okhumudwitsidwa. Umadwala nthenda zamg'onamg'ona ndipo wakhala ukuyenda malo osiyanasiyana koma palibe ndichimodzi chomwe chikukuyendera.
Leronso ndikulakhula ndi moyo wako k*ti gwada pansi ndipo nyengo yako iliyonse umusiyire Mulungu. Iye aliokonzeka kuyakha nyengo zako ndipo palibe chirichonse chimene Chingamulake.
Kaya unaikidwa m'boloto, kaya unanenereredwa za moyo wako k*ti sudzakhala pantchito, sudzakhala ndi mwana, sudzakhala ndi banja, sudzapita chitsogolo lero ndik*ti back to sender mudzina la Yesu!!!
Aliyense amene adakulumikizitsa kuzidole nakumanga lero akuyenera kulandira moto wake wa Mulungu ndipo maunyolo onse ndik*ti aduke mudzina la Yesu.
Khulupirira m'bale lero k*ti Mulungu asitha nyengo zako ndipo tangokhulupirira mwa Yehovah.
Mokupepha, mdalitse wina wake lero ndi uthenga omweu popanga share kuma group 5 okha omwe ulinawo.
Pangani Follow tsambali k*ti muzitha kulandira nkhani ngati izi zomwe zizisitha nyengo zanu konse komwe muliko.
God bless you my brothers and sisters ๐๐๐