Luntha television

Luntha television Luntha TV A Catholic Television located in Malawi. Promoting Spiritual and Integral development of the viewers.

08/08/2025

08/08/2025

LUNTHA TV | NATIONAL EUCHARISTIC CONGRESS (MALAWI) DAY FOUR AFTERNOON | 8 AUGUST 2025

  The Malawi Electoral Commission (MEC) is today receiving a consignment of indelible ink at Kamuzu International Airpor...
08/08/2025




The Malawi Electoral Commission (MEC) is today receiving a consignment of indelible ink at Kamuzu International Airport.

The ink, transported by air, will be used for the upcoming general elections set for September 16, 2025.

Officials from MEC, alongside representatives of various political parties, are on hand to witness its arrival.

(Reported by Patrick Phupha)

08/08/2025


Diabetes on the Rise in Malawi – Many Unaware They Have It

Health experts are warning that diabetes is becoming a “time bomb” in Malawi, with nearly 30% of the population affected — but most don’t even know it.

Dr. Mats Joshua says government is recruiting and training more health workers to screen communities and link patients to treatment. WHO’s Dr. Neema Kimambo adds that over half of diabetic patients in Malawi are undiagnosed, making early detection critical.

Nurse and mental health advocate Maxwell Bonani says the training will help health workers provide better care and break the link between diabetes and mental health challenges.

Early testing can save lives.
(Reported by Judith Ogan)

08/08/2025


Bwalo lamilandu ku south Africa lalamula kuti thupi la mtsogoleli wakale wadziko la Zambia a Edgar Lungu likaikidwe ku Zambia.

Izi ndimalingana ndi chigamulo chomwe oweluza milandu mdziko la South Africa apeleka moomba mkota lelo pofuna kuti olemba nkhani omwe akhala akutsatila mulanduwu ,akhale ndiuthenga ogwilika.

Wolemba Robert Edward.
Video: social media

  Kukumana ndi Ambuye Yesu kudzera Mu Nsembe ya Misa Ambuye Thandizi Vincent Fredrick Mwakhwawa apempha Akhristu ampingo...
08/08/2025


Kukumana ndi Ambuye Yesu kudzera Mu Nsembe ya Misa

Ambuye Thandizi Vincent Fredrick Mwakhwawa apempha Akhristu ampingo wa katolika kuti akulemekeza Nsembe ya Misa komanso kuchita chipembedzo mwa dongosolo.

Bishop Mwakhwawa ati Nsembe mu Nsembe ya Misa muli madalitso chifukwa Akhristu amakumana ndi Ambuye okhala mu kalistia .

Wolemba Emmanuel Chiocha

  Eucharistic Congress Day 4 mass has begun at Maula Cathedral led by Bishop Vincent Frederick Mwakhwawa-Auxiliary Bisho...
08/08/2025


Eucharistic Congress Day 4 mass has begun at Maula Cathedral led by Bishop Vincent Frederick Mwakhwawa-Auxiliary Bishop of Lilongwe Archdiocese! In attendance is Fr. Corrado Maggioni, President of the Pontifical Committee for International Eucharistic Congresses who has come all the way from the Vatican with a message from Pope Leo XIV!

08/08/2025


Nsembe ya Misa

Mwambo wa Nsembe ya Misa wayamba ku msokhano wa Chikondwelero Cha Chaka Ukalistia ku Maula Cathedral Archdiocese ya Lilongwe.

Akutsogolera mwambo wa Nsembe ya Misa ndi Ambuye Thandizi Vincent Fredrick Mwakhwawa , mothandizana ndi Ma Bishop komanso Ansembe.

Wolemba Emmanuel Chiocha

  Sacrament la kulapa ndi machilitsoVigar General Fr Bernard Chipole akumbutsa Akhristu kuti Sacrament la Sacrament la C...
08/08/2025


Sacrament la kulapa ndi machilitso

Vigar General Fr Bernard Chipole akumbutsa Akhristu kuti Sacrament la Sacrament la Chinjano ndi Kulapa ndima Sacrament amachilitso

Fr Chipole akumbutsa Akhristu kuti pa Ubatizo ndi Sacrament la kulapa machimo amakhululukidwa choncho apempha Akhristu kuti azizikonzekerstsa bwino asanalandile Ukalistia.

( Wolemba Emmanuel Chiocha)

Tidziwe za Sacrament la Kulapa ndi Chiyanjano Ndi tsiku lachisanu ku msokhano wa Chikondwelero Cha Ukalistia mu Archdioc...
08/08/2025

Tidziwe za Sacrament la Kulapa ndi Chiyanjano

Ndi tsiku lachisanu ku msokhano wa Chikondwelero Cha Ukalistia mu Archdiocese ya Lilongwe.

Mmawa uno Vigar General a Zomba Diocese Fr Bernard Chipole akuphunzitsa za Sacrament la Chiyanjano ndi Kulapa pokonzekera Kuwalandira Sacrament la Ukalistia.

08/08/2025


Summer class ndiyofunika!

Oyakhulirapo pa nkhani za maphunziro dziko muno Lexon ndalama ndi Lucky mbewe ati ma class apadera(summer class) amathandizira ana kuti achite bwino pamaphunziro awo.

Iwo ati summer school imathandizira mwana kumvetsetsa zina mwa zithu zomwe sanazimvetsetse nthawi yomwe amaphunzira mkalasi.

Iwo anati ngakhale Boma linaletsa masukulu kuti asamapereke maphunziro apa dera nthawi ya tchuthi,zili ndi makolo eni ake kutumiza mwana wawo Kuma phunziro apadera potengera ndi momwe akuchitira mkalasi komanso pamaphuziro ake.

Tchuthi chasukukulu chikuyembezereka kutha pa 22september.
Luntha news updates
Wolemba Fallesy Chizombe

08/08/2025

LUNTHA TV | DAY FOUR: NATIONAL EUCHARISTIC CONGRESS | 8 AUGUST 2025

Address

Luntha Tv, Area 2
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Luntha television posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Luntha television:

Share

Category