Chipini News-Updates

Chipini News-Updates Chipini News-Updates it's a media/news company which provides latest authentic news at Chipini and the surrounding areas. Advertise with us and grow

It is also an advertising media platform.

29/01/2025

Good Morning Followers

18/12/2024

Dear Followers

We would like to inform you that for quite number of months, we have been dormant due to other problems beyond our control.Now everything has back to normal and we will keep you updated.
By Management

01/12/2024

Mbali yakwanuko mvula yagwa, mwazala kale kapena mudakadikirabe

29/07/2022

Anthu olusa atentha nyumba kwa Kamoto

Anthu okwiya ammudzi mwa Kamoto atentha nyumba ya nkulu wina opanga business pa Kamoto pafupi ndi Nansambo school. Bambo dzina lao ndi Akholio izi zachitika kamba koganiziridwa kuti anali m'gulu limene linasowetsa bambo Ena otchedwa Bambo Chafudzika. Bambo Chafudzika anamwalira mwezi wa January ndipo anauka myezi iwiri yapitayi koma nkhope itasinthidwa...Chipini News yapeza zimenezo padakali pano Zina zikamveka tikupatsirani

13/07/2022

Afunireni zabwino zonse Ana amene akuyamba mayeso a PLSCE lero powatchula dzina lawo




27/06/2022

Bambo Muhosha amene anali bambo mfumu mbuyomo pa Chipini Parish amene anapezeka ndi ziwalo za munthu wachi alubino lero kuhigh court Kuzomba Judge wagamula kuti Amuhosha ndi anzawo anayi akagwire ndende kwa zaka Makumi atatu kamba koti anathandizira kupha nzimu wamunthu osalakwa!

14/06/2022

Kodi Za China amajambula Ana Aku Malawi asakuyankhula zinthu zabwino kumagulitsa kwao mwazimva??

Nanga zoti kukuponyedwa ma K5000 mukatola pompo mukumalowa satanic mwazimva ndipo mukukhulupilira???

Timve maganizo anu mu Comment section

Walero!!⚽Guinea🇬🇳🆚🇲🇼 MalawiTime:18:00CAT
09/06/2022

Walero!!⚽

Guinea🇬🇳🆚🇲🇼 Malawi

Time:18:00CAT

05/06/2022

Full Time

Malawi 2-1 Ethiopia

05/06/2022

Malawi 2-1 Ethiopia

Address

Zomba

Telephone

+265884007170

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chipini News-Updates posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Chipini News-Updates:

Share