chippie uwah

chippie uwah Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from chippie uwah, Digital creator, zomba, Zomba.
(15)

I am the multiple award winning content creator from Malawi,I am also the influencer, actor ,the brand ambassador.Making you happy is my priority
For bussiness send email to [email protected] or contact: 0881646589

24/04/2026

Izizi kwanu amapanganso akamachokapo?
Clement Trapence

23/04/2026

Koma abale, zinthu zikuchitika kunja kuno! πŸ’”πŸ™Œ
Nkhani yomwe yakambidwa pa Pamthunzi Podcast yandipatsa chidwi kwabasi. dziko likupita kuti ili? nanga anthu kumagwiliridwa ndi anthu omwe akuyenera kuwatetezaso?
Chomvetsa chisoni ndichokuti Izi zikuchitikira anthu ambiri koma ochepa ndiomwe amabwera poyera. Tiyeni tisakhale chete Amalawi tizitha kumakambirana nkhani zoterezi.
Onerani Nkhani yonse https://youtu.be/tcYsedpS5mM?si=QW-doykxd4lhbsts

πŸ“Ί Mibawa TV – Monday, 9PM
πŸ“» Timveni Radio – Monday, 6PM

Funso nkumati: Kodi abambo amagwiliridwaso kapena ndi akazi okha basi?

Podcast # # BreakTheSilence !πŸ”₯πŸ‘ @

22/04/2026

Kodi ija yomagula ma pant chobisa ija ikanalipo inu Clement Trapence Kwa Abengo- Mesho mukulakwitsa

21/04/2026

Iyiyi nde imakhala yolilitsa akangoti ndikakunenelani kwa akazi anu bansitu , inu mukuoona ngati analakwitsa ndi machippie kapena a truck driver Clement Trapence

21/04/2026

Choncho umakhala kuti watuwa angokuchotsani posewela k50 osakupatsaninso bola mwavina alendo asangalala

20/04/2026

Fareedah wapita chifukwa Sizoona ayi inu Clement Trapence ndi mukulakwitsa

19/04/2026

Komanso ma tax drivers aku Zambia ndapakamwa ngati Uyu Mandunga

19/04/2026

Kumapephera satana azipsa mtima πŸ™

15/04/2026

Kodi izizi zinakuchitikilakoni I kamantha five minutes mu bus kupezekamo wekha Clement Trapence

14/04/2026

Kuphuzitsana galimoto kwabwanji uku eti ?

Atuweni driving school allows you to pay fees in 3 installments, has a 95% passrate, offers you k20,000 if you refer your friends or family, it is located in Blantyre town behind Mount soche hotel next to national library along the mbayani road,

Call or Whatsapp 0997357056

13/04/2026

Who can relate ?

Address

Zomba
Zomba
KEE623

Telephone

+265981937292

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when chippie uwah posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to chippie uwah:

Share