Baibulo Langa Moyo Wanga TV

Baibulo  Langa  Moyo  Wanga TV Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Baibulo Langa Moyo Wanga TV, Digital creator, Zomba.
(4)

Buku Lopatulika
πŸ““πŸ““πŸ“•πŸ“”πŸ“’πŸ“

Gospel Music promoters
Gospel of God Adverts
Preachings
For more Information contact
Andrew Tchona 0996020480/0885421436
Email @gmail.com or @gmail.com

18/09/2025

Mulungu akazangoti kwatha kuzakhala zinthu

18/09/2025

Good morning fam??

17/09/2025

Ngati Akhristu osamatha Mawu zinthu zimasintha

17/09/2025

Makolo tiyeni tiziphuzinsa anawa adakali ang'ono Mawu a Mulungu

17/09/2025

Tiyambe mchochi

MENE MENE TEKEL NDI PARSIN
17/09/2025

MENE MENE TEKEL NDI PARSIN

Ndi nthawitu Ya MavesiπŸ‡²πŸ‡Ό
17/09/2025

Ndi nthawitu Ya MavesiπŸ‡²πŸ‡Ό

17/09/2025

YELIKO WAGWAβ˜‘οΈπŸ‡²πŸ‡Ό

16/09/2025

Bible quiz
Ngati aphonya Mayankho athandidzeni ponyani yankho Lanu mu comment section πŸ‘‡

Muli bwanji mabwana nonse papage pano, ine ndili bwino. Nzina langa ndine blessing nyirenda ndimakhala ku mzuzu hilltop ...
16/09/2025

Muli bwanji mabwana nonse papage pano, ine ndili bwino. Nzina langa ndine blessing nyirenda ndimakhala ku mzuzu hilltop ndipo ndikufuna ntchito as a tax driver ndili ndi license code C1, 3 years of experience, ndimayendesa both manual and automatic vehicles.

School yanga ya driving naphunzila pa chimwemwe driving ku mzuzu konkuno mapepala onse alipo, komanso natianal id ilipo, ndine olimbikila pa ntchito ndipo sindimamwa mowa kapena kusuta. Ndine okonzeka kuyamba ntchito tsiku lina lililonse ngati mwayi ungapezeke chonde chonde ndine munthu okhulupililika kwambiri ndilembeni ntchito mabwana muli pano.

Ndikhala okondwela ndikapeza mwayi umenewu chifukwa ndikungokhala pakadali pano. Ma number anga ndi amenewa 0899542984/0996868037 πŸ™πŸ™

16/09/2025

Masalimo 1:1-16

Address

Zomba

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Baibulo Langa Moyo Wanga TV posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Baibulo Langa Moyo Wanga TV:

Share