Laugh With Geoffrey

Laugh With Geoffrey Wamoyo a zilakwa 🤣✌️

02/01/2026

watch till the end���

02/01/2026
08/08/2023

Kod decoder ya Netflix ilipabwanji 🤔

Only if 😂🤌
27/07/2023

Only if 😂🤌

Not a matter to laugh about 🥺🙏 share the post let's be part of the help as our friend is stranded 🥺👍🏾Pomwe vuto lakusowa...
24/07/2023

Not a matter to laugh about 🥺🙏 share the post let's be part of the help as our friend is stranded 🥺👍🏾

Pomwe vuto lakusowa ntchito likadali lalikulu pakati pa mzika zochuluka maka achinyamata, wachinyamata wina waima pafupi ndi chipata cha likulu la ofesi zaboma ku Lilongwe atanyamula pepala lomwe walembapo kuti akufuna ntchito yoyendetsa galimoto.

Izi zimachitika kwambiri mmaiko omwe ndi otukuka.

by Cassim Aubi

KUIPHULA KOSAYEMBEKEZEREKA.Lethukukhanya  ndi mwana wamkazi wa zaka zitatu zakubadwa wa m'dziko la South Africa amene wa...
15/07/2023

KUIPHULA KOSAYEMBEKEZEREKA.

Lethukukhanya ndi mwana wamkazi wa zaka zitatu zakubadwa wa m'dziko la South Africa amene wagwedeza mma social media kuyambira dzana.

Mwanayu makolo ake anamutuma kugolosale masiku apitawa kukagula bread ndipo pochokera kumeneko anaima pa zithaphwi za madzi n'kumasewera ndi madziwo uku bread uja ali mmanja.Photographer anamujambula mwanayo zithunzi pa chithaphwipo zomwe zinayamba kuyenda mma social media.

Zithunzizo zinapereka chidwi kwa anthu ochuluka maka chifukwa cha mtsangala ya mwanayo komanso nkhope yake yachimwemwe.Zithunzizo zitayenda mma social media zidakafika ku company yopanga bread yo yomwe inapita kwa makolo a mwanayo kukawapempha kuti mwanayo akhale pa billboard atanyamula bread yo ngati advert komanso akhale ambassador wa bread yo.

KUIPHULA KOSAYEMBEKEZEREKA.

14/07/2023

Everyone thinks I'm fine but deep down I need a Gun license n a mental testimonial😉

14/07/2023

Apande zanga zada🥵💔🙌
koma ndadzipaka soap ziyela pompano 🤪😂🙌

23/06/2023

Imagine someone gives you 15million to keep for him and the next day you hears that he has died.

Would that be Good news or Bad news? 🤔

Address

Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Laugh With Geoffrey posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share