Infotainment Malawi

Infotainment Malawi Infotainment Malawi is an independent Malawian online media publication agency.
(3)

Watchuka ali mwana.
15/07/2025

Watchuka ali mwana.

Uyu sanali woyimba wamba. Nyimbo zamphamvu zokhazokha.1978 - 2016 ๐Ÿ•Š๏ธ
15/07/2025

Uyu sanali woyimba wamba. Nyimbo zamphamvu zokhazokha.

1978 - 2016 ๐Ÿ•Š๏ธ

In September, schools open. Kodi mwaganiza kuti mwana wanu apita sukulu yanji? Chaka chatha pa MSCE Kings Foundation was...
15/07/2025

In September, schools open. Kodi mwaganiza kuti mwana wanu apita sukulu yanji?

Chaka chatha pa MSCE Kings Foundation was one of the best performing schools with a 9 points student being the second highest Malawi monse muno and several kids sent to the University.

Komanso ku Kings Foundation samangophunzitsa za mkalasi, they also teach discipline and encourage kids to grow up with the fear of God.

This is the school you want to send your child to.

Pa 22 July pano kuli ma entrance exams kwa ana amene ati akayambe form 1.

Azayamba 9am. Ndipo achitikira ma dera awa;

1. In Ntcheu at Kings Foundation
2. In Lilongwe at Kings Foundation (Rose Academy)
3. In Mzuzu at Ilala Crest Lodge

Examination fee is only MK30,000. Deposit to:

Acc Name: Kings Foundation Schools
Acc Number: 144253358
Bank: NBS, Zomba Branch.

Contacts:

Boys Academy: 0885 636 313
Rose Academy: 0886 282 533
Day School: 0881 611 455
Ilala Crest Lodge Mzuzu:
0881 007 772

Go and show the deposit slip on the day of entrance exams.

Follow them on Facebook for more: https://www.facebook.com/share/1GGedDMrmn/

If Jacques Derrida, a famous French philosopher, was alive, he would celebrate his 95th birthday today.
15/07/2025

If Jacques Derrida, a famous French philosopher, was alive, he would celebrate his 95th birthday today.

ANOTHER REVELATION FROM WELCOME TO MAULA PRISON In the movie 'Welcome To Maula Prison', Mr and Mrs Jaliwa had a daughter...
15/07/2025

ANOTHER REVELATION FROM WELCOME TO MAULA PRISON

In the movie 'Welcome To Maula Prison', Mr and Mrs Jaliwa had a daughter. Her actual name is Mzati Muhezuwa. She is a daughter to a renowned Malawian musician, Chiyanjano Muhezuwa popularly known as Anne Matumbi.

Theresa Phondo ndi wokondwa kulengeza kuti adzapita kukayimba m'dziko la Uganda mumwezi wa Seputembala.Iye adzasangalats...
15/07/2025

Theresa Phondo ndi wokondwa kulengeza kuti adzapita kukayimba m'dziko la Uganda mumwezi wa Seputembala.

Iye adzasangalatsa anthu pamwambo wotchedwa Alive In The Park womwe udzachitike pa 12 Seputembala ku Millennium Park mumzinda wa Lugogo.

Kumwambowu kudzakhalanso katswiri wochokera ku Uganda komweko wotchedwa Pompi.

Mwambo wa Alive In The Park umakonzedwa ndi a Vine Entertainment Group ndipo chaka chino gululi lakwanitsa zilumika zisanu likukonza miyambo ya msangulutso yotere.

15/07/2025

Trophies in 2025โคต๏ธ
Chelsea FC: ๐Ÿ†๐Ÿ†
Utd + City + Gunners: ๐Ÿฅš

TODAY IN SOCIAL MEDIA HISTORY On this day in 2006, a social media platform called Twitter (now X) was launched.Twitter w...
15/07/2025

TODAY IN SOCIAL MEDIA HISTORY

On this day in 2006, a social media platform called Twitter (now X) was launched.

Twitter was created in March 2006 by Jack Dorsey, Noah Glass, Biz Stone and Evan Williams.

Currently, it is owned by South African-born American entrepreneur and politician, Elon Musk.

Woyimba wa chamba cha hip-hop wotchedwa Gomezgani Kambwiri yemwe amangodziwika kuti Toastt walengeza kuti akutulutsa chi...
15/07/2025

Woyimba wa chamba cha hip-hop wotchedwa Gomezgani Kambwiri yemwe amangodziwika kuti Toastt walengeza kuti akutulutsa chimbale chake chatsopano chotchedwa Files.

Chimbalechi chili ndi nyimbo khumi, zisanu ndi zitatu (18) ndipo chidzatuluka Lachisanu likubwerali pa 18 July.

Oyimba ena atatu otchedwa Kim of Diamonds, Sean Morgan ndi Viddix ndi omwe athandizira kuyimba nawo nyimbo zitatu mwanyimbo zomwe zili muchimbalechi.

Good Man, Let It Be, Makaveli, Yaine, Roses, Can You Do That, On Me ndi Time Like This ndi zina mwanyimbo zomwe zili muchimbalechi.

Gift Salika popularly known as Veda Njuchi is celebrating his 25th birthday today. ๐Ÿฅณ
15/07/2025

Gift Salika popularly known as Veda Njuchi is celebrating his 25th birthday today. ๐Ÿฅณ

15/07/2025

TODAY'S FIXTURES (TUE, 15 JULY)

Bournemouth vs Hibernian 1:00 pm
RB Salzburg vs Qarabag 6:00 pm
Celta de Vigo vs Famalicao 6:00 pm
Zwolle vs Kaizer Chiefs 7:00 pm
York FC vs Sheffield Utd 8:00 pm
Accrington vs Everton FC 8:45 pm

YESTERDAY'S RESULTS (14 JULY)


14/07/2025

Penapake atsikanawa amamuchita abuse Ching'aning'ani uja. ๐Ÿ™„

Address

Zomba

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Infotainment Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Infotainment Malawi:

Share

Category