A TCHAMANI

A TCHAMANI Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from A TCHAMANI, Newspaper, Matawale, Zomba.
(7)

STINGY MEN ASSOCIATION OF MALAWI

we offer
* ID
* Certificate
* Newspaper
* Graphic and design (birthday cards, wedding cards, posters etc)

Call/Whatsapp 0881936529

https://youtube.com/?si=-mRj8umQXScblrif

Pamalamuro abungwe la SMAM Pali lamulo linalake limati "Tchamani odha katundu opanda kulipira ndalama." Malingana ndi la...
01/07/2025

Pamalamuro abungwe la SMAM Pali lamulo linalake limati "Tchamani odha katundu opanda kulipira ndalama." Malingana ndi lamuro limeneri matchamani aku Mzuzu awoda sugar lero opanda kupereka kanganyase potsatira kugwa kwa galimoto yonyamula sugar.

01/07/2025

Kutenga zipangizo za ulimi pangongole ku NEEF inu ndikugulitsa double price ndalama inayo kukabweza inayo pathumba 🙌
Mwafikapo eh

KAZEMBE WA BUNGWE LA SMAM MU DZIKO LA KENYA WATIIMILILALelo kulibe video koma titha kulingalira nkhani yomwe ya trenda k...
30/06/2025

KAZEMBE WA BUNGWE LA SMAM MU DZIKO LA KENYA WATIIMILILA

Lelo kulibe video koma titha kulingalira nkhani yomwe ya trenda ku Kenya.

Mayi ali pachithunziyu ndi lawyer, dzina lake Cherotich Keoch. Bwezi lake anali bambo ali pa chithunziyo, Wakili Ke.

Cherotich anali mchikondi zedi ndipo amamulipilira bamboyo school fees poyembekezera kuti adzakwatirana zikadzayenda.

Cherotich anadabwa kuti Wakili atamaliza sukulu, anasowa osapezekanso, kenako anaposita chithunzi cha mkazi wina.

Cherotich anadandaula ku news pepala.

Wakili atawona, wayankha kuti Cherotich asanamize anthu, iyeyo anangomulipilira school fees, koma samamugulira chakudya.
Komanso Wakili wati kupambana kwake ndikochoka kwa Mulungu osati chifukwa choti madam Cherotic anamulipilira.

Sidenote
Mhuu...sidenote lembani ndiinu.

The Jaki Show

30/06/2025

Samalani:- Nyengo ya mayeso ino kumachuluka aphunzitsi a fake, Uchimva china chikuti ndine headteacher pa Mulunguzi Secondary School ndikumenyetsa MSCE preparations pa Whatsapp group kuti mujoine ponyani 10K.

Kumuona yemwe akuti ndi headteacher yo tchamani weniweni wakwa Mayaka. Before kupanga join ma group amenewo fufuzani kaye bwinobwino.

30/06/2025

Ngakhale akulimbikitsa anthu kuti tizisunga ndalama mu phone, koma yodulira yo akuyiona ?

Mapazi anu 🙌

Kafukufuku omwe tapeza lero matchamani ambiri anathamangira patsamba la Google kukapanga search ntchito za Kylie Page.Ky...
30/06/2025

Kafukufuku omwe tapeza lero matchamani ambiri anathamangira patsamba la Google kukapanga search ntchito za Kylie Page.

Kylie Page, waonongetsa chuma cha nkhani nkhani chama tchamani. Matchamani ambiri akhala akuwononga chuma pogula bundle kuti azionelera bwino game ya oyipayo uyu.

SMAM Defence force ikugwira ntchito mwaukadaulo 🔥✊
30/06/2025

SMAM Defence force ikugwira ntchito mwaukadaulo 🔥✊

SDF yagulura asilikari ake ankhondo nsapato zanyuwani kuti asamavutike akarowa ntchire kokasaka ndiwo ndipo Sargent ENOCK HANDALA wabwera poyera kuzathokoza kulikuru la SDF ✊ Poti nsapatozo zawathandiza kuti agwire kasongo ndipo iwo amubweresa kasongoyo kuti SDF igawe kwama tchamani akasuke mkamwa ndipo iwo asindika kuti zipembezo zonse zitha kudya kasongoyu chifukwa iyi sinkhumba Koma kasongo yeyeyeye zikomo kwambili kumpando 🫡A TCHAMANINI

Tchamani wachisodzera ku Silver Strikers FC Chimwemwe Idana, wachoka ku team-yi ndipo walowera ku Zambia ku team ya Zana...
30/06/2025

Tchamani wachisodzera ku Silver Strikers FC Chimwemwe Idana, wachoka ku team-yi ndipo walowera ku Zambia ku team ya Zanaco FC.

Malawi Revenue Authority, mwayambachi ndichibwana iyi siyitha bwino 🙌
30/06/2025

Malawi Revenue Authority, mwayambachi ndichibwana iyi siyitha bwino 🙌

Lawyer wathu uja umuthandizire Tchamani wathu uyu 🙌
30/06/2025

Lawyer wathu uja umuthandizire Tchamani wathu uyu 🙌

Zabwino zonse ma members athu a SMAM omwe akulemba mayeso a MSCENthawi yolemba meyesoyi mukuloredwa kugwiritsa ntchito t...
30/06/2025

Zabwino zonse ma members athu a SMAM omwe akulemba mayeso a MSCE

Nthawi yolemba meyesoyi mukuloredwa kugwiritsa ntchito transport ya galimoto popita kolemba mayeso. Chakudya idyani ndithu mokwanira bwino.

Ustingy muzayambiraso after jiya.

30/06/2025

Bungwe loyendetsa Mayeso ku SMAM lati pakadali pano palibe candidate yemwe wapereka examination fee kufikira tsiku lalero. Mayeso akuyamba pa 2 July.

Address

Matawale
Zomba
TCHAMANI

Website

http://www.atchamani41.com/, https://www.youtube.com/@atchamani

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when A TCHAMANI posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category