
30/08/2025
Ma business ang'onoang'ono koma opedzetsa profit yochuluka.
📌- Samusa
Zofunika pa samusa
Flour 1kg
Mice meat 1kg
Spices 3 bottles
Cooking oil 2 litters
0nion 1kg
Capital
Flour K3,000
Mince meat K20,000
Spices K1,500
Cooking oil K18,500
Onion. K2,000
TOTAL K45,000
1 kg ya flour imatilutsa samusa 100
Mtengo WA samusa ndi 700-1000 each malingana ndi ma customer Ako
K700x100 =K70,000
mafuta ophikira umaphikira samusa 200-250 pa 2 litters iliyonse.
Mince meat osagula ya economy simalimba,komaso sikometsa samusa always kumagula yopanga mafuta ija.
Samusa wamkulu sakoma,kumapanga WA size,azikhala kadya ubwelele.
That's how you can make money in samusa business just be consistency in this,mudzandiyamika.
Mwakoma nonse.
Utilah📌