Che Masi

Che Masi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Che Masi, Media/News Company, Zomba.

Aliyese azinena zomwe akuona kwa nyamata mukumuona apayi wakuzombaa.zikuchitika ndithu
17/10/2025

Aliyese azinena zomwe akuona kwa nyamata mukumuona apayi wakuzombaa.
zikuchitika ndithu

Malipoti osatsimikizika kuchokera ku Chipani cha DPP ati akuluakulu a Chipanichi  akhumudwa ndi ganizo la mtsogoleri wa ...
16/10/2025

Malipoti osatsimikizika kuchokera ku Chipani cha DPP ati akuluakulu a Chipanichi akhumudwa ndi ganizo la mtsogoleri wa Chipanichi a Peter Mutharika losankha a Sameer Suleiman ngati yemwe apikisane pa mpando wa sipikala wa Nyumba ya Malamulo

Izi zikudza pomwe akuti ambiri anasankha Dr Ben Phiri ngati womwe akuyenera kupitkisana pa mpandowu

A Phiri akuti anali atayamba kale kukonzekera pa mpandowu




Mrs Namadingo
16/10/2025

Mrs Namadingo

Rise for Phoka is a Community Based Foundation which is in Livingstonia,Rumphi. The organisation focuses on community ac...
16/10/2025

Rise for Phoka is a Community Based Foundation which is in Livingstonia,Rumphi. The organisation focuses on community activities,education and elderly companionship among others, I f you have time visit them,learn and know more about them.
Today on 16 October, Rise for Phoka is cerebrating World Food Day with the theme
visit their website at www.riseforphoka.org
email: [email protected]

Ndalama zokwana K25 million ndi zomwe zagwiritsidwa ntchito kujambula kanema wotchedwa Chitomero yemwe muli atengambali ...
13/10/2025

Ndalama zokwana K25 million ndi zomwe zagwiritsidwa ntchito kujambula kanema wotchedwa Chitomero yemwe muli atengambali odziwika bwino monga Ginte, Phwedo komanso Mphatso Machira.

Ndalamayi anaipereka ndi mkulu wina wa mdziko la America kuti zonse zokhudza kanemayu yemwe muli atengambali oposa 40 ziyende bwino.

Phwedo yemwe analemba nkhani ya kanemayu wati kanemayu alunjika kwambiri pa nkhani ya chikhalidwe cha dziko lino ndipo yajambulidwa malo akumudzi kokha.

Phwedo watinso mkanemayu Ginte achita khalidwe lake lopezeka malo a akabanga (Mowa) pomwe iyeyu ndi Mphatso Machira asintha makhalidwe awo.

Woyimba Malita ndi yemwe wakonza kanemayu ndipo naye watenganso mbali mkanemayu.

Kanema wa Chitomero atulutsidwa mwezi wa mawa koma kachidutsa kake katuluka masabata awiri akubwerawa.

Neria Chikhosi, Yvonne Scott, Pamela mwenisungo, Everisto payesa ndi enanso mwa atengambali omwe ali mkanemayu.

Ati Mudzi omwe ajambulira kanema uyu adachita kumanga okha.Iyi ndi Movie ya ‘CHITOMERO’ imene muli oyimba zachikhalidwe,...
13/10/2025

Ati Mudzi omwe ajambulira kanema uyu adachita kumanga okha.

Iyi ndi Movie ya ‘CHITOMERO’ imene muli oyimba zachikhalidwe, Malita ndi akatswiri opanga mafilimu odziwika bwino m’Malawi monga Phwedo, Ginte komanso Mphatso Machira.

Chitomero ndi mwambo umene wakhala ukudziwika bwino kwambiri mudzaka za mbuyo kotero Chitomero ndi movie yomwe ikufotokoza za Chikhalidwe cha chiMalawi.

Filimu imeneyi ikhala ikutuluka mu November 🎥

 President APM ndi Chipani cha DPP chasankha Hon Suleman ngati candidate wa Speaker ya nyumba yamalamulo.
12/10/2025



President APM ndi Chipani cha DPP chasankha Hon Suleman ngati candidate wa Speaker ya nyumba yamalamulo.

A Malawi ambiri amusowa Timothy Mtambo, akungofuna atatulukiraMawu amodzi kwa Comrade
12/10/2025

A Malawi ambiri amusowa Timothy Mtambo, akungofuna atatulukira

Mawu amodzi kwa Comrade

12/10/2025

Oyimba, Joe Gwaladi, wati akutulutsa chimbale chatsopano momwe muli nyimbo khumi.

Gwaladi wati a-Malawi ayembekezere nyimbo zabwino.



Malawi NewsBoma kudzera ku ofesi ya  mkulu wowona za nthambi komanso kampani za boma lati laimitsa kaye ndondomeko zonse...
12/10/2025

Malawi News

Boma kudzera ku ofesi ya mkulu wowona za nthambi komanso kampani za boma lati laimitsa kaye ndondomeko zonse zokhudza kulemba anthu ntchito komanso kugura katundu ku kampanizi zomwe boma lapitali linayamba.

Malingana ndi kalata yomwe wasainira ndi mkulu wa ofesiyi Mayeso Kazombo izi ndi kuyambira pa 7 October chaka. Mu kalatayi a Kazombo ati ganizoli ladza pofuna kuwonesetsa kuti zonse zokhudza ndondomekozi ziwunikidwe bwino.

  Member of Parliament for Nkhata Bay Central, Symon Vuwa Kaunda, has donated 30 iron sheets valued at K6 million to Kal...
12/10/2025



Member of Parliament for Nkhata Bay Central, Symon Vuwa Kaunda, has donated 30 iron sheets valued at K6 million to Kalambwe CCAP Church under the Livingstonia Synod, Nkhata Bay Vestry.

Address

Zomba

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Che Masi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share