Mupacho

Mupacho Mulungu Palibe Chomulaka

Apart from money, what else makes you extremely happy ??
17/07/2025

Apart from money, what else makes you extremely happy ??

OFUNA SAUSAGE YOKOMA AJA TIKUMANE MU LIMBE   MK6000 pure beef sausage.📱 0997190042You have all the rights to get me arre...
17/07/2025

OFUNA SAUSAGE YOKOMA AJA TIKUMANE MU LIMBE

MK6000 pure beef sausage.
📱 0997190042

You have all the rights to get me arrested if the sausages doesn’t taste good 😌

KIDNEY STONES ( miyala yamu impso)✓iyi ndi miyala yomwe imatha kupezeka nkati mwa kidney(impso)  yanu. Miyalayi ndi mich...
17/07/2025

KIDNEY STONES ( miyala yamu impso)

✓iyi ndi miyala yomwe imatha kupezeka nkati mwa kidney(impso) yanu. Miyalayi ndi michere( salts & minerals) yomwe yaundana pamodzi. Miyalayi imatha kukhala ing'ono ing'ono ngati mchenga pena ngati kabulu kachimanga
✓ miyala yamu impso imapangidwa pamene mu mkodzo wanu muli michere yambiri( eg calcium, oxalate uric acid kuposa madzi omwe angasungunule michereyo

KODI CHIMAYAMBISA MIYALAYI NDICHANI?
✓ kuchepekela Kwa madzi m'thupi; ichi ndichoyambisa chachikulu, ngati simukumwa madzi okwanila ndekuti mikozo yanu ikhala ndi michere yambiri kuposa madzi zomwe zipangise kuti michere ija yiundane pamodzi ndikupanga miyala
✓ madyedwe; kudya zakudya za mchere kwambiri, sugar komaso red meat( nyama ya mbuzi or ya ng'ombe kwambiri)
✓ngati m'banja mwanu alipo kapena Kwa makolo anu aliko anadwalapo, pamakhalaso ka mwayi koti inuso m***a kudwala
✓kunenepa koonjeza kumasoneza mlingo wa uric acid amene atha kuyambisaso miyala yamu impso
✓makhwala ena atha kuyambisaso miyala monga ma diuretics, ma antibiotics ena komaso ma antacid omwe amakhala ndi calcium

ZIZINDIKILO ZA KIDNEY STONES
✓ Kupweteka ku nsana mmusi, pansi pa mimba pamene kupwetekekaku kumazayendelera kufika m'mphechepeche( m'ma groin)
Kumva kupweteka mukamakoza
✓kufuna kukonza pafupipafupi
✓ kukonza mikozo ya magazi
✓mikozo yotulusa fungo
✓kumva nseru komaso kusanza
✓ thupi kutentha/ kumva kuzizizdwa

KODI TINGAPEWE BWANJI MA KIDNEY STONES?

✓ Kumwa madzi pafupipafupi ( 2-3 liters pa tsiku) kuonesesa kuti mikozo yanu ikale ya pale yellow kapena ya clear( yopanda mtundu), dziwani kuti tea komaso coffee atha kuyambisaso ma kidney stones ndikunenawa
NOTE; lemon juice amathandiza kuti michere isapangidwe m'ma ipso athu
✓kuthila mchere wamlingo wabwino
✓kuchepesa kudya nyama tafotokoza( red meat, madzira)
✓ chepesani thupi pamene mukuona kuti weight yanu yakwela
✓chepesani kumwa makhwala musanaonane ndi dokotala

Dziwani kuti pamene miyalayi ili yaying'ono itha kusungunuka ngati mukumwa madzi moyenelera
Mukaona zizindikilo tanenazi ndibwino kupita kuchipatala mwachangu

NGATI MWAPINDULA NAWO UTHENGAWU ITANANI ANZANU APANGE FOLLOW Mupacho

16/07/2025

12:00 😊😊 oziwa mavuto ake wadzuka kale

THE REMAINS OF HOTEL MASONGOLA IN ZOMBA
16/07/2025

THE REMAINS OF HOTEL MASONGOLA IN ZOMBA

Mumapanga business yanji Tiyipange promote ife ka price  pang'ono ....Azanuwotu sikuti ndi okhwima ai kma business yawo ...
16/07/2025

Mumapanga business yanji

Tiyipange promote ife ka price pang'ono ....Azanuwotu sikuti ndi okhwima ai kma business yawo amapanga promote

Tinakumana bwanji?
16/07/2025

Tinakumana bwanji?

China!!Pomwe ife tikuvutika ndi mphepo nthawi ino ya winter ,amzathu ku China akuvutika ndi dzuwa chifukwa ndi nthawi ya...
16/07/2025

China!!

Pomwe ife tikuvutika ndi mphepo nthawi ino ya winter ,amzathu ku China akuvutika ndi dzuwa chifukwa ndi nthawi yawo ya summer.

Popewa kugula mafuta ozitetezera ku dzuwa (SPF 30+) anthu ambiri ayamba kugwilitsa ntchito masamba kumadziphimba kumaso like face masks,guys ndalama ikuvuta wina aliyense 🤣🤣🤣🤣

Masamba ake akumasankha aakulu okuti akhoza kuwaphimba bwino bwino kufikira nkhosimu.
Ena amagwilitsa Umbrella hats koma pano ikutrenda ndi ya masamba yi.

I wounder kuti masamba amenewa ali nawo ochuluka motani chifukwa akhozaso kumaononga chilengedwe.

Follow Mupacho and share for more Stories.

Mu zaka za 1950s bambo wina  ochokera ku kiribati  anapita kokawedza mwatsoka anasowa,( kusochera osadziwa direction yak...
16/07/2025

Mu zaka za 1950s bambo wina ochokera ku kiribati anapita kokawedza mwatsoka anasowa,( kusochera osadziwa direction yakwawo) ndipo after stranded for days
mafunde anamukankhira ku Island ina yotchedwa Namdrik Atoll Island komwe sanapeze any means yakuti akhoza kubweleranso kwawo.

M'baleyu anakhazikika kumeneko mpakana kupeza mkazi ndikukwatira konko kupanga family ndithu yaikulu

Nephew wa bambowa kuchokera ku Kiribati nayenso anaganiza zopita kokawedza ndipo mwatsoka anapezekanso kuti wasokonekera sakudziwa komwe amachokera, ndipo mnyamatayu anakhala mmadzi kwa masiku 33 akudya nsomba zaziwisi ndi kumwa madzi amvura,

koma chodabwitsa ndi chakuti mafunde anamukankhiranso malo omwe aja anakankhira Uncle ake aja,

Ndipo anthu aku Namdrik Atoll Island anamulandira mwansangala ndikumusunga Koma atayamba kumufunsa mafunso komwe wachokera zapezeka kuti, ndi mwana ochokera kumudzi omwe kunachokera abambo aja ndipo ndi mwana wa achemwali abambo aja ...

Ku Kiribati 🇰🇮 anthu analira kale maliro kuti m'bale wawo anafera madzi koma sankadziwa kuti adakali ndi moyo.
Choyambilira chomwe chinawapangitsa chidwi anthuwa ndi native language yawo imene mnyamatayu amalankhula inali exactly ndi ya malume ake aja.

After half century, fate brought two generations of the same family together in the most incredible way imaginable.

Nkhaniyi ikutiphunzitsa kuti Yehova ali ndi njira zake zofukula zinsinsi zobisika ndikuzibweletsa poyera.

Taganizani ma families awiliwa tsiku limene anapezana kunali chisangalalo chotani atazindikira kuti m'bale wao yemwe anasowa mu 1950s alinso ndi family ina ku dziko lina ...



Follow Mupacho and share for more incredible stories of fate and family.

The best sausages !! You won’t regret A pack of 5 sausages only at k6000 and we also supply in large quantities 📍 Blanty...
16/07/2025

The best sausages !! You won’t regret
A pack of 5 sausages only at k6000 and we also supply in large quantities
📍 Blantyre Chirimba - dorvic hotel
You have all the rights to get me arrested if the sausages doesn’t taste good 😌
Call or WhatsApp 0997190042

Ndiye kuli kadziko kena kake kotchedwa Turkmenistan 🇹🇲 limene Lili located ku Central Asia ndipo linapanga border ndi ma...
16/07/2025

Ndiye kuli kadziko kena kake kotchedwa Turkmenistan 🇹🇲 limene Lili located ku Central Asia ndipo linapanga border ndi maiko awa :

Kazakhstan 🇰🇿 ku North, Uzbekistan 🇺🇿 ku North East and east,
Afghanistan 🇦🇫 ku ku South East ,Iran ku South komaso Caspian sea 🌊 ku West.

It's a landlocked country with a rich cultural heritage and history known for its natural gas reserves,

Ka dziko kameneka mu chaka cha 1971 akuti panali ma blander amene anapangika ndipo pipe line ina ya gas inaphulika nde poti ndi kumalo kumene amasungirako gas anangoganiza zoyatsako moto ndi cholinga choti gas ⛽️ uja asaononge chilengedwe komaso miyoyo ya anthu

But kuchokera nthawi imeneyo kufikira lero lino moto sunazime umangoyaka .

Maiko omwe anakazungulira kadziko kamene akuoneka ngati ndi antopola okho okha

Kuteroko malowa anangowapatsa dzina lakuti "Gateway to Hell"

Maganizo awo anali oti moto uzima gas akangotha koma mpakana pano kudakali moto ndipo anangosandutsako malo a tourism kumene anthu amapita kukaonako.

Follow Mupacho nd share for more inspiring stories.

Address

Usatove

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mupacho posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share