Za Ife

Za Ife Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Za Ife, Digital creator, Africa, Kampala.

 Panali kusamvana pakati pa asilikari a MDF komanso apolisi ku Zomba.(Video kuma comment) Tapeza kuti msilikari wina wau...
16/02/2026


Panali kusamvana pakati pa asilikari a MDF komanso apolisi ku Zomba.
(Video kuma comment)

Tapeza kuti msilikari wina waudindo anamangidwa ndi apolisiwa kamba koyendetsa galimoto yake ataledzera koma izi sizinasangalatse asilikari ena omwe anapita malo amene apolisiwa amachita chipikisheni magalimoto kukabweza chipongwe.

Kanemayu akuonetsa apolisiwa atagwaditsidwa kwinaku akuuzidwa kuti apepese.

President waku Uganda Yoweri Museveni akumayenda mu chi Glass kwachuluka adani kuopa kumuombera
27/01/2026

President waku Uganda Yoweri Museveni akumayenda mu chi Glass kwachuluka adani kuopa kumuombera

22/01/2026

atelo ATI nkuntchisi tu kumeneko anthu akuyenda mmi nseu ya golide

14/01/2026

😃😃

Madness Entertainment yati yasayina chinanso. Uyu ndi Nava Madness, mwana wa dzaka  21 yemwe Madness yalengeza  kuti  wa...
13/01/2026

Madness Entertainment yati yasayina chinanso. Uyu ndi Nava Madness, mwana wa dzaka 21 yemwe Madness yalengeza kuti watengedwa kukhala modzi wa oyimba wawo.

Congratulations and all the best Nava 👏
khangati uyu ndi replacement yawina uja 😂

13/01/2026

akati ng'onA 😂

Address

Africa
Kampala

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Za Ife posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share