Poet CJ Guwa

Call Directions Website Contact the business

Poet CJ Guwa ABWEZI MWANDIONA SON OKWERA NDEGE ✈️❤️ ACHISALE Social media reporter

Multi-award-winning poet from Malawi. Telling African stories through poetry and art.

Zikomo Awards nominee • Young Achievers Africa winner 🏆 -2024 MBC EOY nominee.

15/10/2026

Amayi awa muli nkhofi ati osataya mimba atsikana

15/10/2026

Wagulira mpunga, salu ndi zina mayi ake tangokumana ku Nyanja ndi nyamatayi ochokera Dowa.

15/10/2026

Odala Anakubala Iweyo. Happy mother's day to all moms 🙏🥳

14/10/2026

Kwacha mayanga 2pin osawapatsa while last year nati next year koma maluzi😭
Happy mothers day mom

14/10/2026

Zativuta makolo maluzi masiku sakoma onse
Iyi yokha mothers day simupanga nawo mom😭

13/10/2026

Ona Scorchers iwe 🔥🥳🇲🇼

Owakwera ndi omwewa azimayiwa 😆Scorchers yasambitsa Zimbabwe zigoli 7 kwachilowere pa kwawo komko. Team ya dziko ndi iyi...
13/10/2026

Owakwera ndi omwewa azimayiwa 😆Scorchers yasambitsa Zimbabwe zigoli 7 kwachilowere pa kwawo komko. Team ya dziko ndi iyi basi 🔥🇲🇼🥳

Oyimba odziwika bwino chamba cha a mapiano Zeze Kingston tsopano wakwanitsa 1 miliyoni folowazi.Iye wakhala oyimba wa na...
13/10/2026

Oyimba odziwika bwino chamba cha a mapiano Zeze Kingston tsopano wakwanitsa 1 miliyoni folowazi.

Iye wakhala oyimba wa namba 9 kukhala ndi owatsatira pa tsamba la Mchezo fesibuku. Amene anayambitsa ndi DR Namadingo kupeza owatsatira ochuluka chomcho.

Posachedwapa Zeze adabweretsa tsutso pomwe adagawa ndalama pa siteji. Izi zinachitika boma la Lilongwe komwe kunali show ya Kelly Kay. Anthu ena anati kumwaza ndalama ndi mulandu, ena amati sanalakwitse.

Congratulations 50 billion gang Zeze

By Bambo Chisale

13/10/2026

Therere lobala limakoma kudya osaphika kungothira tomatoes and anyezi

Address

4590
Mohali
96713

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Poet CJ Guwa posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Poet CJ Guwa:

Shortcuts

Share