Jame Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Jame, Digital creator, Bloemfontein.

28/07/2026

Good morning

24/07/2026
22/07/2026

kuyimba nyimbo ya gun boss

  MAPHUNZIRO AZACHIPEMBEZO OMWE ANA AMAPHUNZIRA OCHOKERA KUMAYIKO AKU ALUYA(ARAB) NDI OSATHANDIZA-TRAOREM'tsogoleri wa d...
21/07/2026


MAPHUNZIRO AZACHIPEMBEZO OMWE ANA AMAPHUNZIRA OCHOKERA KUMAYIKO AKU ALUYA(ARAB) NDI OSATHANDIZA-TRAORE

M'tsogoleri wa dziko la Burkina Faso Ibrahim Traore wati maphunziro a zipembedzo omwe amaperekedwa kwa ophunzira a m'dzikolo m'mayiko ena ngati kwa a Luya (achi Arab) ndi osathandiza kutukula dziko lawo.

Malingana ndi zomwe yalemba nyumba yofalitsa nkhani ya DW Africa a Traore ati ophunzira pafupifupi 1,000 akuphunzira Sharia ndi malamulo achisilamu ku Saudi Arabia m'malo mophunzira luso laukadaulo lomwe lingathe kufunika potukula dziko lawo.

Pakadali pano a Traore ati boma lawo likukonzekera zobweretsa ophunzira onse kwawo omwe anapita kunja ndicholinga chokaphunzira zachipembezo ndi malamulo achisilamu.

Kupatula izi m'tsogoleriyu wachenjeza ena amene angakane kubwelera kwawo kamba koti atha kutaya ufulu wawo wokhala m'dziko la Burkina Faso.

Mawu a Traore abwera pambuyo poti dziko la Burkina Faso likufuna likhazikitse lamulo latsopano lokhudza ufulu wachipembedzo lomwenso likhudzenso kwambiri m'chitidwe wachipembedzo ndi kutsindikanso ufulu wolambira.

Wotanthauzira nkhaniyi kuchokera kutsamba la DWAfrica: David Somba-Mzuzu

Akuluwa yapweteka 😂😂😂 Anakakonda ring imeneyi atayivala Messi
20/07/2026

Akuluwa yapweteka 😂😂😂 Anakakonda ring imeneyi atayivala Messi

20/07/2026

chichewa

basitu world cup ija yatha
20/07/2026

basitu world cup ija yatha

The Chairman of the Board of Directors,  Dr Benson Tembo and all the Directors of the Board, Director General of MBC Mr ...
18/07/2026

The Chairman of the Board of Directors, Dr Benson Tembo and all the Directors of the Board, Director General of MBC Mr Brian Banda, Directors, Management and Staff of the Malawi Broadcasting Corporation wishes His Excellency the President of the Republic of Malawi Prof. Arthur Peter Mutharika all the best on his Birthday today.

Inspiring The Nation

16/07/2026

Tamvani chichewa umu🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

ANATHA ZAKA 39 ALI CHIKOMOKEREJean Pierri Adams osewera mpira wakale wa France komanso timu ya PSG anabadwa mu chaka cha...
08/07/2026

ANATHA ZAKA 39 ALI CHIKOMOKERE

Jean Pierri Adams osewera mpira wakale wa France komanso timu ya PSG anabadwa mu chaka cha 1948.. Koma mu 1982 anakhala ali chikomokere (Coma) kufikira 2021..

Adams anapita ku chipatala kuti akathandizidwe mwendo wake omwe anavulala mu March 1982 ali ndi zaka 34 koma kumeneko anapeza anthu ogwira ntchito pa chipatala cha Lyon akunyanyala ntchito koma surgery inapitilira ngakhale kunali ogwira ntchito m'modzi kuyang'anira odwala 8 mothandizana ndi wazachipatala wapasukulu.. Anthu awiri azachipatalawa anapanga zolakwitsa zambiri... Anampatsa mankhwala oti agone kwa maola ochepa (anaesthetic) koma Adams sanadzukemso.. Iye anapezeka ndi nthenda ya mtima (Cardiac arrest) komanso kuonongeka kwa ubongo.. Koma Mulungu anamukonda Adams anamusiyabe ndi moyo ndipo anatulutsidwa mchipatala patatha miyezi 15 koma ankakhala pa life supporting machine.. Izi zinali chomwechi popeza amkaganiza ngati atha kuzadzukamso.. Adams anakhala akusamalidwa panyumba ndi mkazi wake ngakhale anali pa life supporting machine kwa nthawi yomseyi.. Mu 2021 ali ndi zaka 73 aku banja anachita kuvomereza kuti atha kuthimitsano life supporting machine m'bale wawo sangazitolelemso ngati momwe ankaganizira pachiyambi..


Mkaziyu analimso wa chikondi koma chfukwa enawa zaka 39 sangakhale akudwazika matenda oti simukuyankhulanapo mpaka atapempha divorce chaka chomwecho

Address

Bloemfontein

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Jame posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share