Mama Jubeki

Mama Jubeki ☆ Actress ☆ Businesswoman ☆Master of Ceremonies☆

I love spreading awareness &positive vibes🫶🫶🫶
(1)

16/09/2026

Hello Neba👋

Hello Neba👋Pheeeeee ku tchuthi, ndachita kuyiwalilatu ndi mayina ankhalamba omwe🤣🤣🤣🤣🤣
16/09/2026

Hello Neba👋

Pheeeeee ku tchuthi, ndachita kuyiwalilatu ndi mayina ankhalamba omwe🤣🤣🤣🤣🤣

Hello Neba👋Koditu kachakumwa kosangalalira sikowawa kokhakokha,makamaka kwaife omwe fantafe  tisamafinyike🤣🤣🤣🤣🤣🤣
14/09/2026

Hello Neba👋

Koditu kachakumwa kosangalalira sikowawa kokhakokha,makamaka kwaife omwe fantafe tisamafinyike🤣🤣🤣🤣🤣🤣

14/09/2026

Hello Neba👋

Tiyeni ku lunch Neba😋😋😋

14/09/2026

Hello Neba👋

🤣🤣🤣🤣🤣🤣🤣

Hello Neba👋Khalamba zandisowa ndithu😂😂😂 Koma nane ndi Munthu thupi limafunika kulipumusa, let me enjoy my leave💃💃💃💃💃💃💃💃
14/09/2026

Hello Neba👋

Khalamba zandisowa ndithu😂😂😂 Koma nane ndi Munthu thupi limafunika kulipumusa, let me enjoy my leave💃💃💃💃💃💃💃💃

13/09/2026

Hello Neba👋

Timapangana interview ndi Patricia kuseliku kuti ndi driverdi? nanga umboni upotse apa✍️✍️✍️✍️✍️✍️

Hello Neba👋MWAYI SUSOCHERA,MULUNGU AKALEMBA WALEMBA BASI✍️✍️✍️✍️Ntchito ya driver wankazi wapezeka munthu, nditamusakha ...
13/09/2026

Hello Neba👋

MWAYI SUSOCHERA,MULUNGU AKALEMBA WALEMBA BASI✍️✍️✍️✍️

Ntchito ya driver wankazi wapezeka munthu, nditamusakha mu comment section, tayakhulana ku inbox ndikupatsa number yanga, koma chodabwisa ndichakuti anandilembelapo kufuna ntchito ya u driver ndipo analemba last year pa 28 December 2025,lero mu September 2026 ntchito yapezeka, ndaona kukhala umboni ndithu, Mulungu ali ndi nthawi yake🙏

Congratulations Patricia 💃💃💃💃💃

Hello Neba👋MWAYI WANTCHITO YA MUNTHU WANKAZI DRIVER KOMASO AZIKA CLEANER-SANDTON(JOHANNESBURG) Hello mama tafusani munth...
13/09/2026

Hello Neba👋

MWAYI WANTCHITO YA MUNTHU WANKAZI DRIVER KOMASO AZIKA CLEANER-SANDTON(JOHANNESBURG)

Hello mama tafusani munthu pa Group ngati alipo Malawi wankazi oziwa kuyendetsa galimoto kupita ndi Ana ku school kukawatenga komanso kupanga cleaning pakhomopo,ntchitoyi ndi stay in kutuluka ndi fortnight akufunika mawa 11 koloko koma interview ikakhala yoyendetsa ngalimotoyo

Starting salary :R8000

Note:Chonde yekhayo oziwa kuyendetsa galimoto alembe mu comment SECTION,ntchito sindigulitsa zongothandizana izi , first come first save✍️✍️✍️✍️✍️✍️

Address

Boksburg
1459

Telephone

+27634371919

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mama Jubeki posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mama Jubeki:

Shortcuts

Share