Malawi trends news

Malawi trends news Fan page

16/08/2026

Izi nde mzamuwanthu tsopano aaa ndi gone ine 🙄😡

FUNERAL PROGRAMME FOR THE LATE BRIAN BANDADirector General, Malawi Broadcasting Corporation (MBC)The funeral programme f...
08/08/2026

FUNERAL PROGRAMME FOR THE LATE BRIAN BANDA
Director General, Malawi Broadcasting Corporation (MBC)

The funeral programme for the late Mr. Brian Banda, Director General of the Malawi Broadcasting Corporation, is as follows:

Sunday, 9 August 2026
The body of the late Mr. Brian Banda will be taken from Mthunzi Mortuary at 11am to Word of Faith Church in Chilobwe, Blantyre, where a a Church service will be held.

Monday, 10 August 2026, the late Brian Banda will be laid to rest at M’banda Village, Chileka, a few kilometres after Bakili Muluzi International Airport, Blantyre.

May his soul rest in eternal peace.😭💔

ANANDIUZA KUTI ANDINYENGERA AKAZI ANGA NDI ANA NDIKAPANDA KUWAPATSA NDALAMA - DICKSON BAMUSIBambo Dickson Bamusi, azaka ...
05/08/2026

ANANDIUZA KUTI ANDINYENGERA AKAZI ANGA NDI ANA NDIKAPANDA KUWAPATSA NDALAMA - DICKSON BAMUSI

Bambo Dickson Bamusi, azaka 44, kuchoka ku Lilongwe Area 25, auza a police kuti akuba omwe anafika kunyumba kwawo lero cha m'ma past midnight, anawauza kuti agwililira ana awo ndi mkazi wawo ngati mkulu yi sapeleka ndalama.

Iwo ati amagona, kenaka anamva kakalakakala Cha ku sitting room. Kudzuka kuti akapange check, anangozindikila apatsidwa mbama pomwe amalowa mu corridor ndipo anagwa. Wakuba yemwe ananyamula chikwanje ndi mzake anawauza kuti adzuke.

"Wina yo amafuna kuti andikhape koma mzake anamuletsa ponena kuti sakufuna kuona magazi." Atero a Dickson.

Iwo apitilizs kuti akubawo analipo 6 ndipo anawapatsa ndalama zokwana 164,000 zomwe anali nazo mnyumba mo, chifukwa sanafune kuti ana awo omwe ali ndi zaka 13 komanso 9 agwililidwe.

Kupatula ndalama, akuba wo atenga TV, Sound bar, ma phone awo komanso ndiwo mu fridge.

Akuba wo analowela window la ku dining room pogwiritsa ntchito jeke wa scissors kukanula ma burglar bar.

Anyamata a zikwanje a MCP aku Zambia amuwonetsa zokuda Joseph mkasa wa kumeneko
04/08/2026

Anyamata a zikwanje a MCP aku Zambia amuwonetsa zokuda Joseph mkasa wa kumeneko

04/08/2026

Ma kadeti achipani cholamura ku Zambia cha UPND akuntha oyimba General Kanene ndi zikwanje pomwe amafuna aziyimba ku msonkhano wa chipani chotsutsa.. Pakadali pano wagonekedwa ku chipatala cha Chawama Level 1.

Iyi ndi survival of the fittest.. Game ya wadya mtoliro

Mozambique
04/08/2026

Mozambique

Kabaza operators take care
04/08/2026

Kabaza operators take care

04/08/2026

Three suspects have been arrested in Limpopo, South Africa, after they were allegedly found in possession of two stolen vehicles.

According to preliminary reports, the suspects were intercepted by South African authorities while allegedly attempting to move the stolen vehicles out of the country. The vehicles had reportedly been reported stolen.

Among those arrested were two Malawian nationals, aged 36 and 40, according to the preliminary information available.

The suspects are expected to face charges relating to the alleged theft and possession of stolen motor vehicles. Police investigations are continuing to establish where the vehicles were stolen from and whether the suspects are connected to a wider vehicle-smuggling network.

Authorities have recovered the vehicles as investigations continue.

A Malawi awiri, ndi modzi wa ku South Africa, amangidwa ndi "anti motor" police ya ku Limpopo, South Africa, atagwidwa a...
04/08/2026

A Malawi awiri, ndi modzi wa ku South Africa, amangidwa ndi "anti motor" police ya ku Limpopo, South Africa, atagwidwa ataba galimoto za mtundu wa Nissan Navara Pro-4X zokwana ziwiri.

Mmodzi mma a Malawi omwe agwidwa wa ndi a Gifted Banda aku Mangochi.

Mtengo wa galimoto zonse ziwiri ndi R1.9 million (300 million Kwacha).

Directorate of Road Traffic and Safety Services azepuleni ana osava awa.
03/08/2026

Directorate of Road Traffic and Safety Services azepuleni ana osava awa.

Address

Cape Town

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi trends news posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share