Innoma-Journalist

Innoma-Journalist Arts & Entertainment | Sports | Gossips | Politics | Developments | PR & Marketing | Research | Consultancy
(2)

23/08/2025

Arsenal itaphwasamula Manchester United pa Old Trafford, lero yakutumulanso Leeds United 5 kwa chetechete.

Kuseliku Akuti ingowapasani league🙌😄

Log Table Ili motere lero
23/08/2025

Log Table Ili motere lero

FT: Mighty Tigers 0 Vs 1 Silver Strikers George Chikooka ndamene wasankhidwa Man of the Match
23/08/2025

FT: Mighty Tigers 0 Vs 1 Silver Strikers

George Chikooka ndamene wasankhidwa Man of the Match

Bullets igona pamwamba pa Noma usiku unoChitipa vs BulletsFT: Chitipa United 0-2 FCB Nyasa Big Bullets
23/08/2025

Bullets igona pamwamba pa Noma usiku uno

Chitipa vs Bullets
FT: Chitipa United 0-2 FCB Nyasa Big Bullets

Ambiri akuti iyi yatha iyi87'| Babatunde Adepoju Chitipa 0-2 Bullets
23/08/2025

Ambiri akuti iyi yatha iyi

87'| Babatunde Adepoju

Chitipa 0-2 Bullets

23/08/2025

75 mins wakaaaaaaa

Mighty Tigers 0-1 Silver Strikers
Binwell Katinji

President Dr Lazarus Chakwera wati, boma lake liyesesa kuti lichite zitukuko zomwe mfumu yaikulu Tsabango apempha.A Tsab...
23/08/2025

President Dr Lazarus Chakwera wati, boma lake liyesesa kuti lichite zitukuko zomwe mfumu yaikulu Tsabango apempha.

A Tsabango, anayamba ndikuyamikila boma pa zitukuko zomwe lachita mzaka zisanu zapitazi kuphatikizirapo madzi, miseu, zipatala, ma sukulu ndi zina.

Pakanali pano, iwo apempha kuti mseu ochoka ku 23 kudutsa Kwa Chiuzira awaganizire Tala, komanso madzi amu mipopi afike pa chipatala.

Photos By: Innoma-Journalist 📸

Anyamata omwe akugaya Chitipa uku ndi awa.46 mins, Chitipa 0-1 Bullets
23/08/2025

Anyamata omwe akugaya Chitipa uku ndi awa.

46 mins, Chitipa 0-1 Bullets

23/08/2025

Khooo!
Amutikita
FT: Man City 0-2 Spurs

Ma game ena onse kuli chete chete pa half time, kupatuka ya Chitipa vs Bullets yokha basi komwe ampasa mbama akwawo pomp...
23/08/2025

Ma game ena onse kuli chete chete pa half time, kupatuka ya Chitipa vs Bullets yokha basi komwe ampasa mbama akwawo pompo.

Half Time update TNM Super League 👇

Half Time 🚨Chitipa United 0-1 FCB Nyasa Big Bullets
23/08/2025

Half Time 🚨

Chitipa United 0-1 FCB Nyasa Big Bullets

23/08/2025

Man City, mukulora kufela pa nyumba zoona?
86'
Man City 0-2 Spurs

Address

Shumani Street
Lilongwe
7140

Telephone

+27786221611

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Innoma-Journalist posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Innoma-Journalist:

Share