Zavuta

Zavuta Only truth

Komatu ngati ziri choncho Malawi anaopsa;Sad News 💔 😭 Ma report akusonyeza kuti Bambo Kalembera omwe akuluakulu ena achi...
13/09/2026

Komatu ngati ziri choncho Malawi anaopsa;

Sad News 💔 😭

Ma report akusonyeza kuti Bambo Kalembera omwe akuluakulu ena achipani cha UTM anawagulira njinga ya moto apezeka atafa atasowa kwa masiku awiri.

Akuluakulu ena a UTM motsogozedwa ndi a Felix Njawala anasonkhetsa ndalama kuti mkuluyu aguliridwe njinga ya moto pokondwa ndimomwe amavalira makaka achipanichi akamayendetsa njinga yake ya kapalasa.

13/09/2026

SIMBA FC 6-1 MANOMA

kuposa wa azimayi

Koma andale mumaona ngati a Malawi ndife opusa?Chipani cha Malawi Congress (MCP) chapepesa ku zipani zomwe chinali nazo ...
13/09/2026

Koma andale mumaona ngati a Malawi ndife opusa?

Chipani cha Malawi Congress (MCP) chapepesa ku zipani zomwe chinali nazo pa mgwirizano pa nthawi ya chisankho cha 2020 kufika pomwe chinapamba, kuphatizapo cha UTM, pa zomwe chati sichinakwiritse kukwanitsa pa mgwirizanowu.

Mneneri wachipanichi, a Jessie Kabwira walankhula pomwe mwazina wati chipanichi pali zina zomwe sichinachite bwino.

"Pali zinthu zomwe tidayenera kuti tipange bwino. Tiuze mtundu wa aMalawi taphunziranso ndi mamistakes [zolakwika] amene tinapanga. Kumene kuli UTM umvetsetse kuti pa zimene sitinachite bwino ilandire kupepesa kwathu.

Bola chilungamo chioneke Makomiti apadera omwe amayenera kukhazikitsidwa kuti afufuze nkhani zosiyanasiyana ayamba ayimi...
13/09/2026

Bola chilungamo chioneke

Makomiti apadera omwe amayenera kukhazikitsidwa kuti afufuze nkhani zosiyanasiyana ayamba ayimitsidwa kaye, izi ndi malingana ndi ofesi ya sipikala wanyumba ya malamulo.

Kalata yomwe ofesiyi yatulutsa yati, pali chiletso chochokera kubwalo lamilandu chomwe chaperekedwa pa 4 September, 2026 chokhudza nkhaniyi.

Mwazina, kalatayi yatinso sipikala wanyumba ya malamulo a Sameer Suleman anali ndi mkumano ndi mtsogoleri wa dziko lino a Peter Mutharika dzulo loweruka pa 12 September, 2026 ndipo ati mbali ziwirizi zimalemekeza kusiyana kwa mphamvu kwa nthambi zitatu zikuluzikulu

13/09/2026

Big shout out to my newest top fans! Kinlos Naonje, Mavuto Thunyani

Zina ukamva Mai Ndiuzayani ali ndi zaka 36 apha mwana wawo wazaka 15 pomupatsa chakudya Cha poison ku Chiradzulu.Mwana w...
12/09/2026

Zina ukamva

Mai Ndiuzayani ali ndi zaka 36 apha mwana wawo wazaka 15 pomupatsa chakudya Cha poison ku Chiradzulu.

Mwana wa Mai wa anali osokonekela ubongo ndiye amapanga zovutitsa kwambiri. Ndiye Iwo auza a police kuti zinawatopetsa, anthu amawaseka, kumangokhalira kulipila katundu yemwe mwana wawoyi wawononga.

Pamudzi pano anthu akukwatira ndikukwatiwa,nanga inu mukuti bwa?
12/09/2026

Pamudzi pano anthu akukwatira ndikukwatiwa,nanga inu mukuti bwa?

11/09/2026

one mistake

Zakhalanso bwanji? Ku Malawi kuno Pena kumazasekesa zochitika zipani nde mbweeee koma zochitika mbwelera.
11/09/2026

Zakhalanso bwanji?

Ku Malawi kuno Pena kumazasekesa zochitika zipani nde mbweeee koma zochitika mbwelera.

Zina ukamvaBoma lati ligulitsa sitima zake zapa madzi zomwe zakhala nthawi yaitali zisakugwira ntchito.Sitimazi ndi Mpas...
11/09/2026

Zina ukamva

Boma lati ligulitsa sitima zake zapa madzi zomwe zakhala nthawi yaitali zisakugwira ntchito.

Sitimazi ndi Mpasa ndi Nkhwazi zomwe ziri pa doko la Monkey Bay, komanso sitima ya Mcheni yomwe ili m'boma la Nsanje.

Address

Chartworth
Cape Town
524

Telephone

+265994253209

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Zavuta posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share