Teyona

Teyona Content creator
Fun
Celebrity stories
Crime stories around the world🫣

Akuti apha akazawo powamenya ndi mpini wa khasu usiku wathawu akugona chifukwa amawaganizila kuti akuwazembera mwa nseri...
10/12/2025

Akuti apha akazawo powamenya ndi mpini wa khasu usiku wathawu akugona chifukwa amawaganizila kuti akuwazembera mwa nseri 🙌awamanga a police

10/12/2025

I got over 20 reactions on one of my posts last week! Thanks everyone for your support! 🎉

HUMANITY " RULES:!1. If you open it, close it.2. If you turn it on, turn it off.3. If you unlock it, lock it.4. If you b...
04/12/2025

HUMANITY " RULES:!
1. If you open it, close it.
2. If you turn it on, turn it off.
3. If you unlock it, lock it.
4. If you break it, fix it.
5. If you can't fix it, call someone who can.
6. If you borrow it, return it.
7. If you use it, take care of it.
8. If you make a mess, clean it up.
9. If you move it, put it back.
10. If it belongs to someone else and you want to use it, get permission.
11. If you don't know how to operate it, leave it alone.
12. If it doesn't concern you, don't mess with it.
♥️💛💚

03/12/2025

Before a woman packs her bags and leaves PHYSICALLY, she had already left EMOTIONALLY and MENTALLY a long time ago 👌

Apolice aku South Africa agwira mbava zomwe ndi nzika za maiko a Zimbabwe komanso Malawi zomwe zinaba galimoto mukuiona ...
02/12/2025

Apolice aku South Africa agwira mbava zomwe ndi nzika za maiko a Zimbabwe komanso Malawi zomwe zinaba galimoto mukuiona apayi yomwe amafuna kulumpha nayo border nkumapita nayo ku Zimbabwe. Izi zachitika ku Limpopo

Apa sibasi la 40 lakwana amalawi anzanga tiyeni tiphunzire kulimbikira kuba sikwabwino kufuna kulemera mwachangu koma mukutiipitsira Mbiri aziti Amalawi ndi akuba

Mwadzuka bwanji lero pa 1 December 2025 achibale?
01/12/2025

Mwadzuka bwanji lero pa 1 December 2025 achibale?

30/11/2025

🤣🤣🤣🤣koma nde pantie tu

All is set! Usiku uno, Movie ya Chitomero ayiwonetsa koyamba ku BICC ( Lilongwe ) kuyambila 6pm. Akatelo, week yamawa pa...
30/11/2025

All is set! Usiku uno, Movie ya Chitomero ayiwonetsa koyamba ku BICC ( Lilongwe ) kuyambila 6pm. Akatelo, week yamawa pa 5 December , filimuyi ukaonetsedwa ku Blantyre ( Apollo Arcade ).

Ma ticket atha kugulidwa kudzela airtel money kapena ku venue konko

Ineyo ndili pa number 4 po achibale kkkkk inuyo mumadya bwanji fupa😂
30/11/2025

Ineyo ndili pa number 4 po achibale kkkkk inuyo mumadya bwanji fupa😂

Happy birthday to 12 August babies 🥳
12/08/2025

Happy birthday to 12 August babies 🥳

Address

Durban

Telephone

+27847852647

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Teyona posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share