09/11/2025
MA SKILLS AMENE MUYENERA KUPHUNZIRA
Abale dziko lik*tsogola Maka pa nkhani ya technology. Ndipo ife tili k*tali kwambiri Maka pa nkhani ya luso pa internet.
Dziko likulemekeza anthu amene Ali ndi luso ndik*thekera kopanga chinthu from the scratch.
Masiku ano almost chilichose cha pa internet chikugwiritsidwa nthito ndi AI.
Zinthu monga:
Writing Designing Web developing Video creating etc
Ndipo mwa zonsezi zimatheka ndi prompt basi, kungolemba zomwe mukufunazo pa Ai tool ndipo zimakubweretselani.
MUNGALEMBE BWANJ PROMPT?
Kulemba prompt kunali kovutilapo nthawiyo koma now chilichonse chili simple kwambiri. Chatgpt imapanga generate prompt komanso ma scenes ngati mukufuna kupanga create ma videos.
Chofunika ndikungokhala ndi idea ya chinthu chomwe mukufunacho ndipo chatgpt izapanga analyze bwinobwino.
Ziwani k*ti ku internet kuli nthito zomwe mungapange popereka luso lanu m***a kugwira nthito za freelance Kuma website monga upwork.
Ndipo uku kumakhala nthito monga.
-web designing
-video editing
-writing
-translating
-software developer
-cybersecurity specialist
Ndipo ndizofunika k*ti tiphunzire zinthu ngati zimenezizi.