Uncle Gaxy

Uncle Gaxy Machedza okhaokha with Uncle Gaxy ๐Ÿ™ ๐Ÿ˜Ž

Wadzuka bwanji neba๐Ÿ˜๐Ÿ˜๐Ÿ˜
09/09/2026

Wadzuka bwanji neba๐Ÿ˜๐Ÿ˜๐Ÿ˜

08/09/2026

Anthu mukuchimwa๐Ÿ˜†๐Ÿ˜‚๐Ÿคฃ
Uncle Gaxy

Iweyo zoona ndalama mpaka kusunga mu pant๐Ÿ˜๐Ÿ™„Uncle Gaxy
08/09/2026

Iweyo zoona ndalama mpaka kusunga mu pant๐Ÿ˜๐Ÿ™„
Uncle Gaxy

Nde ukudikira chani Mwalo mopanga follow apa๐Ÿ™„๐Ÿ˜      Uncle Gaxy
08/09/2026

Nde ukudikira chani Mwalo mopanga follow apa๐Ÿ™„๐Ÿ˜
Uncle Gaxy

Mwadzuka bwanji kuli konse komwe muli?      Uncle Gaxy
08/09/2026

Mwadzuka bwanji kuli konse komwe muli?
Uncle Gaxy

Mphunzirani kubweza satana kwa amzanu๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚   Uncle Gaxy
07/09/2026

Mphunzirani kubweza satana kwa amzanu๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚

Uncle Gaxy

Ndikukuuzilantuni๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚ musazadabweUncle Gaxy
07/09/2026

Ndikukuuzilantuni๐Ÿคฃ๐Ÿ˜‚ musazadabwe
Uncle Gaxy

๐Ÿ”ด STEP 1: CHOYAMBA DZIWANI CHIFUKWA CHOMWE DASHBOARD YANU ILI REDMutu wa post:๐Ÿ”ด RED DASHBOARD? MUSACHITE MANtha! โ€” STEP ...
07/09/2026

๐Ÿ”ด STEP 1: CHOYAMBA DZIWANI CHIFUKWA CHOMWE DASHBOARD YANU ILI RED
Mutu wa post:

๐Ÿ”ด RED DASHBOARD?

MUSACHITE MANtha! โ€” STEP 1
Zomwe tiziphunzira:
Ngati Professional Dashboard yanu ili ๐Ÿ”ด RED, musayambe kungopanga ma post ambiri osadziwa chomwe chikuyambitsa vutolo.

Chinthu choyamba ndi KUPEZA VUTO.
Yang'anani zinthu izi pa dashboard yanu:

โœ… Views โ€“ Kodi anthu akuonera content yanu mokwanira?

โœ… Engagement โ€“ Kodi anthu akukonda, commenting ndi kugawana ma post anu?

โœ… Followers โ€“ Kodi mukulandira followers atsopano?

โœ… Content performance โ€“ Ndi ma post ati omwe akuyenda bwino komanso ati sakuyenda?

โœ… Monetization โ€“ Kodi pali ma policy kapena eligibility issues?

๐Ÿ’ก Musamangoyang'ana mtundu wa dashboard. Yang'anani zomwe dashboard ikukuuzani.
Iyi ndi Step 1 yokha. Mu Step 2 tidzaphunzira mmene tingadziwire chomwe chikubweretsa vuto pa page yathu. ๐Ÿ”ฅ
๐Ÿ‘‡ Comment โ€œSTEP 2โ€ ngati mukufuna tipitirize limodzi.
๐ŸŸข Ndipo mukafuna next step

Mwadzuka bwanji kuli konse komwe muli?     Uncle Gaxy
07/09/2026

Mwadzuka bwanji kuli konse komwe muli?

Uncle Gaxy

๐Ÿšจ YOUR FACEBOOK DASHBOARD IS RED?DON'T GIVE UP โ€” LET'S TURN IT AROUND! ๐ŸŸขCaption:Your dashboard being RED does not mean y...
06/09/2026

๐Ÿšจ YOUR FACEBOOK DASHBOARD IS RED?
DON'T GIVE UP โ€” LET'S TURN IT AROUND! ๐ŸŸข
Caption:
Your dashboard being RED does not mean your Facebook journey is over.
Starting tomorrow, Uncle Gaxy is starting a step-by-step series called:
๐Ÿ”ด RED DASHBOARD TO GREEN โ€” STEP BY STEP
We will look at: โœ… What makes a dashboard perform badly
โœ… Content quality
โœ… Engagement
โœ… Watch time
โœ… Original content
โœ… Posting strategy
โœ… Audience retention
โœ… Monetization requirements
โœ… Common mistakes creators make
We won't rush. One step at a time.
If your dashboard is RED, follow this series and let's learn together. ๐ŸŸข
COMMENT โ€œREDโ€ if you want to follow the journey from Step 1.

3.9 Inali Red 3 weeks ago koma pano simungakhulupilire kuti ili green chifukwa chotsata malamuro a Facebook
Uncle Gaxy

Address

Durban

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Uncle Gaxy posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share