The Nyasaland Post

The Nyasaland Post _International news updates
_Sports updates
_Jokes
_Entertainment
(2)

Awa ndi ma team a mpira mu Africa muno omwe alowa nawo mu round of 32 mu World Cup imeneyi. (1). Ghana(2). Senegal (3). ...
27/06/2026

Awa ndi ma team a mpira mu Africa muno omwe alowa nawo mu round of 32 mu World Cup imeneyi.
(1). Ghana
(2). Senegal
(3). Cape Verde
(4). South Africa
(5). Egypt
(6). Ivory Coast
(7). Morocco
It's time for AFRICA!!!...😎💃💪

Senegal yachitika mwayi kuseliku, 😏 yapambana kulowa mu round of 32. Mtibu wa dzuro wazigori uja wathandiza team ya Sene...
27/06/2026

Senegal yachitika mwayi kuseliku, 😏 yapambana kulowa mu round of 32. Mtibu wa dzuro wazigori uja wathandiza team ya Senegal kufika mu ndime imeneyi. Athokoze Mulungu ndithu chifukwa alowako mwamwayi ndithu.

Mbappe ali ndi moyo wabwino, takhara tikuwona akuwayamikira amzake monga Messi ndi Ronaldo kuti awiriwa ali pamwamba zed...
26/06/2026

Mbappe ali ndi moyo wabwino, takhara tikuwona akuwayamikira amzake monga Messi ndi Ronaldo kuti awiriwa ali pamwamba zedi ngakhale kuti nayenso ndi dolo. Alibe jelasi amzake akamachita bwino konse ayi. Let's love one another. 😘

26/06/2026

Full Time
France 4:1 Norway
Senegal 5:0 Iraq

Dembeleee! 3 goals yekha in less than 35 minutes.  What a striker!
26/06/2026

Dembeleee! 3 goals yekha in less than 35 minutes. What a striker!

🚨 Vinícius Júnior on why Cristiano Ronaldo is the GREATEST OF ALL TIME in his opinion: “I don’t just look at talent. I l...
26/06/2026

🚨 Vinícius Júnior on why Cristiano Ronaldo is the GREATEST OF ALL TIME in his opinion: “I don’t just look at talent. I look at the whole picture”.

“Cristiano has proven it in England, Spain, Italy, and Portugal. Different leagues, different teammates, different generations… but always the same: GOALS, TROPHIES, AND RECORDS” 🏆

“He transformed hard work into an art form. His discipline, sacrifice, and consistency are also talents”.

“That’s why, for me, Cristiano Ronaldo is the best footballer of ALL TIME”

Mchemwali wanu Temwa akuti mumuvotere kuseliku 😏. Ati wapangidwa nominate mu ESPY best soccer player limodzi ndi Messi n...
26/06/2026

Mchemwali wanu Temwa akuti mumuvotere kuseliku 😏. Ati wapangidwa nominate mu ESPY best soccer player limodzi ndi Messi ndiye akuti chonde muvotereni apambane Link waika pa Page yake.

Mpweteko wa lero, 😏Mbappe vs Haaland ziliko lero...👇👇
26/06/2026

Mpweteko wa lero, 😏Mbappe vs Haaland ziliko lero...👇👇

Mudzi wanji uwu amzathu amene mwayenda kwambiri ku Malawi-ko? So interesting...😏
25/06/2026

Mudzi wanji uwu amzathu amene mwayenda kwambiri ku Malawi-ko? So interesting...😏

Mpira wa Canada ndi Switzerland ndi phala lenileni lomwe anyamata akulitereka ndikumapungulirana aliyense mu kapu🍺 pa gr...
24/06/2026

Mpira wa Canada ndi Switzerland ndi phala lenileni lomwe anyamata akulitereka ndikumapungulirana aliyense mu kapu🍺 pa ground pompo. Ingogonani mudzuke 12 koloko mupeza mpira weniweni kawawa monga Morocco vs Hait komanso Brazil vs Scotland. Zinazi zikutayitsani nthawi chabe ndi michabwa iyi yakumana. Onse akumakanika kuchinya man to man ndi goal keeper ma team onsewa koma ayi ndithu osachinya olo zosewera zawo ndi matope enieni chithaphwi, ndi mikute iyi kagoneni.😏

Address

Limbe
Blantyre
4052

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The Nyasaland Post posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to The Nyasaland Post:

Share